Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Uthenga Wabwino Wolembedwa ndi Yohane

Machaputala

1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 11 12 13 14 15 16 17 18 19 20 21

Mitu

  • 1

    • Mawu anakhala munthu (1-18)

    • Umboni umene Yohane Mʼbatizi anapereka (19-28)

    • Yesu ndi Mwanawankhosa wa Mulungu (29-34)

    • Ophunzira oyambirira a Yesu (35-42)

    • Filipo komanso Natanayeli (43-51)

  • 2

    • Ukwati ku Kana; anasandutsa madzi kukhala vinyo (1-12)

    • Yesu anayeretsa kachisi (13-22)

    • Yesu amadziwa zimene zili mumtima mwa munthu (23-25)

  • 3

    • Yesu ndi Nikodemo (1-21)

      • Kubadwanso (3-8)

      • Mulungu anakonda dziko (16)

    • Umboni womaliza wa Yohane wokhudza Yesu (22-30)

    • Wochokera kumwamba (31-36)

  • 4

    • Yesu ndi mayi wa ku Samariya (1-38)

      • Muzilambira Mulungu “motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi” (23, 24)

    • Asamariya ambiri anakhulupirira Yesu (39-42)

    • Yesu anachiritsa mwana wamwamuna wa mtumiki wa mfumu (43-54)

  • 5

    • Munthu wodwala anachiritsidwa ku Betizata (1-18)

    • Yesu anapatsidwa ulamuliro ndi Atate wake (19-24)

    • Akufa adzamva mawu a Yesu (25-30)

    • Maumboni okhudza Yesu (31-47)

  • 6

    • Yesu anadyetsa anthu 5,000 (1-15)

    • Yesu anayenda pamadzi (16-21)

    • Yesu ndi “chakudya chopatsa moyo” (22-59)

    • Ambiri anakhumudwa ndi mawu a Yesu (60-71)

  • 7

    • Yesu anapita ku Chikondwerero cha Misasa (1-13)

    • Yesu anaphunzitsa kuchikondwerero (14-24)

    • Anthu anali ndi maganizo osiyanasiyana okhudza Khristu (25-52)

  • 8

    • Atate anachitira umboni za Yesu (12-30)

      • Yesu ndi “kuwala kwa dziko” (12)

    • Ana a Abulahamu (31-41)

      • “Choonadi chidzakumasulani” (32)

    • Ana a Mdyerekezi (42-47)

    • Yesu ndi Abulahamu (48-59)

  • 9

    • Yesu anachiritsa munthu amene anabadwa wosaona (1-12)

    • Munthu amene anachiritsidwa anafunsidwa mafunso ndi Afarisi (13-34)

    • Afarisi anali osaona (35-41)

  • 10

    • Mʼbusa ndi makola a nkhosa (1-21)

      • Yesu ndi mʼbusa wabwino (11-15)

      • “Ndili ndi nkhosa zina” (16)

    • Ayuda anakumana ndi Yesu ku Chikondwerero Chopereka Kachisi kwa Mulungu (22-39)

      • Ayuda ambiri anakana kukhulupirira (24-26)

      • “Nkhosa zanga zimamva mawu anga” (27)

      • Mwana ndi wogwirizana ndi Atate (30, 38)

    • Anthu ambiri akutsidya la Yorodano anakhulupirira (40-42)

  • 11

    • Imfa ya Lazaro (1-16)

    • Yesu anatonthoza Marita ndi Mariya (17-37)

    • Yesu anaukitsa Lazaro (38-44)

    • Chiwembu choti aphe Yesu (45-57)

  • 12

    • Mariya anathira mafuta pamapazi a Yesu (1-11)

    • Yesu analowa mumzinda mwaulemerero (12-19)

    • Yesu ananeneratu za imfa yake (20-37)

    • Kupanda chikhulupiriro kwa Ayuda kunakwaniritsa ulosi (38-43)

    • Yesu anabwera kudzapulumutsa dziko (44-50)

  • 13

    • Yesu anasambitsa mapazi a ophunzira ake (1-20)

    • Yesu ananena kuti Yudasi adzamupereka (21-30)

    • Lamulo latsopano (31-35)

      • “Ngati mukukondana” (35)

    • Ananeneratu kuti Petulo adzamukana (36-38)

  • 14

    • Yesu ndi njira yokhayo yotifikitsa kwa Atate (1-14)

      • “Ine ndine njira, choonadi ndi moyo” (6)

    • Yesu analonjeza mzimu woyera (15-31)

      • ‘Atate ndi wamkulu kuposa ine’ (28)

  • 15

    • Fanizo la mtengo wa mpesa weniweni (1-10)

    • Lamulo loti tizisonyeza chikondi ngati cha Khristu (11-17)

      • ‘Palibe amene ali ndi chikondi chachikulu kuposa chimenechi’ (13)

    • Dziko limadana ndi ophunzira a Yesu (18-27)

  • 16

    • Ophunzira a Yesu akhoza kuphedwa (1-4a)

    • Ntchito ya mzimu woyera (4b-16)

    • Chisoni cha ophunzira chidzasanduka chisangalalo (17-24)

    • Yesu anagonjetsa dziko (25-33)

  • 17

    • Pemphero lomaliza la Yesu ali ndi atumwi ake (1-26)

      • Anthu adzapeza moyo wosatha akadziwa Mulungu (3)

      • Akhristu sali mbali ya dziko (14-16)

      • “Mawu anu ndi choonadi” (17)

      • “Ine ndachititsa kuti iwo adziwe dzina lanu” (26)

  • 18

    • Yudasi anapereka Yesu (1-9)

    • Petulo anagwiritsa ntchito lupanga (10, 11)

    • Yesu anamupititsa kwa Anasi (12-14)

    • Petulo anakana Yesu koyamba (15-18)

    • Yesu anaonekera pamaso pa Anasi (19-24)

    • Petulo anakana Yesu kachiwiri ndi kachitatu (25-27)

    • Yesu anaonekera pamaso pa Pilato (28-40)

      • “Ufumu wanga si wamʼdzikoli” (36)

  • 19

    • Yesu anakwapulidwa ndi kuchitiridwa zachipongwe (1-7)

    • Pilato anafunsanso Yesu (8-16a)

    • Yesu anamukhomerera pamtengo ku Gologota (16b-24)

    • Yesu anakonza zoti mayi ake asamaliridwe (25-27)

    • Imfa ya Yesu (28-37)

    • Kuikidwa mʼmanda kwa Yesu (38-42)

  • 20

    • Manda opanda kanthu (1-10)

    • Yesu anaonekera kwa Mariya wa ku Magadala (11-18)

    • Yesu anaonekera kwa ophunzira ake (19-23)

    • Tomasi anakayikira koma kenako anakhulupirira (24-29)

    • Cholinga cha mpukutuwu (30, 31)

  • 21

    • Yesu anaonekera kwa ophunzira ake (1-14)

    • Petulo anatsimikizira kuti amakonda Yesu (15-19)

      • “Dyetsa ana a nkhosa anga” (17)

    • Tsogolo la wophunzira wa Yesu amene ankamukonda kwambiri (20-23)

    • Mawu omaliza (24, 25)