Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

A7-G

Zinthu Zikuluzikulu Zimene Yesu Anachita Ali Padziko Lapansi—Utumiki Womaliza wa Yesu mu Yerusalemu (Gawo 1)

NTHAWI

MALO

ZIMENE ZINACHITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

33, Nisani 8

Betaniya

Yesu anafika ku Betaniya kutatsala masiku 6 kuti Pasika achitike

     

11:55–12:1

Nisani 9

Betaniya

Anamuthira mafuta mʼmutu

26:6-13

14:3-9

 

12:2-11

Betaniya-Betefage-Yerusalemu

Analowa mu Yerusalemu monga wopambana, atakwera bulu

21:1-11, 14-17

11:1-11

19:29-44

12:12-19

Nisani 10

Betaniya-Yerusalemu

Anatemberera mtengo wamkuyu; anayeretsanso kachisi

21:18, 19; 21:12, 13

11:12-17

19:45, 46

 

Yerusalemu

Ansembe aakulu ndi alembi anakonza chiwembu kuti aphe Yesu

 

11:18, 19

19:47, 48

 

Mawu a Yehova anamveka; Yesu ananeneratu za imfa yake; kusakhulupirira kwa Ayuda kunakwaniritsa ulosi

     

12:20-50

Nisani 11

Betaniya-Yerusalemu

Mtengo wamkuyu umene unafota

21:19-22

11:20-25

   

Yerusalemu, mʼkachisi

Anakayikira ulamuliro wa Khristu; fanizo la ana aamuna awiri

21:23-32

11:27-33

20:1-8

 

Mafanizo: alimi oipa, phwando la ukwati

21:33–22:14

12:1-12

20:9-19

 

Anayankha mafunso okhudza Mulungu ndi Kaisara, kuuka kwa akufa komanso lamulo lalikulu kuposa onse

22:15-40

12:13-34

20:20-40

 

Anafunsa zokhudza Khristu

22:41-46

12:35-37

20:41-44

 

Anadzudzula alembi ndi Afarisi

23:1-39

12:38-40

20:45-47

 

Mkazi wamasiye anapereka zopereka

 

12:41-44

21:1-4

 

Phiri la Maolivi

Chizindikiro cha kukhalapo kwake

24:1-51

13:1-37

21:5-38

 

Mafanizo: anamwali 10, matalente, nkhosa ndi mbuzi

25:1-46

     

Nisani 12

Yerusalemu

Atsogoleri anakonza zopha Yesu

26:1-5

14:1, 2

22:1, 2

 

Yudasi anakonza zopereka Yesu

26:14-16

14:10, 11

22:3-6

 

Nisani 13 (Lachinayi masana)

Pafupi ndi Yerusalemu, ndi mkati mwake Anakonzekera

Pasika womaliza

26:17-19

14:12-16

22:7-13

 

Nisani 14

Yerusalemu

Anadya Pasika limodzi ndi atumwi

26:20, 21

14:17, 18

22:14-18

 

Anasambitsa mapazi a atumwi ake

     

13:1-20