Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

B12-B

Wiki Yomaliza ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Gawo 2))

Yerusalemu ndi Madera Ozungulira

  1. Kachisi

  2.   Munda wa Getsemane (?)

  3.    Nyumba ya Bwanamkubwa

  4.   Nyumba ya Kayafa (?)

  5.   Nyumba imene Herode Antipa ankakhala (?)

  6. Damu la Betizata

  7. Dziwe la Siloamu

  8.   Holo ya Khoti Lalikulu la Ayuda (?)

  9.   Gologota (?)

  10. Munda Wamagazi (?)

     Sankhani tsiku:  Nisan 12 |  Nisan 13 |  Nisan 14 |  Nisan 15 |  Nisan 16

 Nisani 12

MADZULO (Masiku a Ayuda amayamba ndi kutha dzuwa litalowa)

M’MAWA

  • Yesu ndi ophunzira ake

  • Yudasi anakonza zoti apereke Yesu

MADZULO

 Nisani 13

MADZULO

M’MAWA

  • Petulo ndi Yohane akukonzekera Pasika

  • Yesu ndi atumwi ake ena anafika madzulo

MADZULO

 Nisani 14

MADZULO

  • Anadya Pasika ndi atumwi ake

  • Anasambitsa mapazi a atumwi ake

  • Anauza Yudasi kuti achoke

  • Anayambitsa mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye

  • Anaperekedwa n’kumangidwa m’munda wa Getsemane ( 2)

  • Atumwi anathawa

  • Anaimbidwa mlandu ndi Khoti Lalikulu la Ayuda ( 4)

  • Petulo anakana Yesu

M’MAWA

  • Anakaonekeranso m’Khoti Lalikulu la Ayuda ( 8)

  • Anapita naye kwa Pilato ( 3), kenako kwa Herode ( 5), n’kubwereranso kwa Pilato ( 3)

  • Anaweruzidwa kuti aphedwe ndipo anaphedwera ku Gologota ( 9)

  • Anafa cha m’ma 3 koloko madzulo

  • Anachotsa mtembo wake n’kukauika m’manda

MADZULO

 Nisani 15 (Sabata)

MADZULO

M’MAWA

  • Pilato anavomereza zoika alonda pamanda a Yesu

MADZULO

 Nisani 16

MADZULO

  • Anagula zonunkhiritsa zina zopaka mtembo wa Yesu

M’MAWA

  • Anaukitsidwa

  • Anaonekera kwa ophunzira ake

MADZULO