Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

B8

Kachisi Amene Solomo Anamanga

  1. Mbali za Kachisi

  2. 1 Malo Oyera Koposa (1 Maf. 6:16, 20)

  3. 2 Malo Oyera (2 Mbiri 5:9)

  4. 3 Zipinda Zapadenga (1 Mbiri 28:11)

  5. 4 Zipinda Zam’mbali (1 Maf. 6:5, 6, 10)

  6. 5 Yakini (1 Maf. 7:21; 2 Mbiri 3:17)

  7. 6 Boazi (1 Maf. 7:21; 2 Mbiri 3:17)

  8. 7 Khonde (1 Maf. 6:3; 2 Mbiri 3:4) (Kutalika kwake sikudziwika bwinobwino)

  9. 8 Guwa Lansembe Lakopa (2 Mbiri 4:1)

  10. 9 Nsanja Yakopa (2 Mbiri 6:13)

  11. 10 Bwalo Lamkati (1 Maf. 6:36)

  12. 11 Thanki Yosungira Madzi (1 Maf. 7:23)

  13. 12 Zotengera Zokhala ndi Mawilo (1 Maf. 7:27)

  14. 13 Khomo Lam’mbali (1 Maf. 6:8)

  15. 14 Zipinda Zodyera (1 Mbiri 28:12)