Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

A7-B

Zinthu Zikuluzikulu Zimene Yesu Anachita Ali Padziko Lapansi—Chiyambi cha Utumiki wa Yesu

NTHAWI

MALO

ZIMENE ZINACHITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

29, chakumapeto kwa chaka

Mtsinje wa Yorodano kapena ku Betaniya wakutsidya la Yorodano

Ubatizo ndi kudzozedwa kwa Yesu; Yehova analengeza kuti Yesu ndi Mwana wake ndipo anamuvomereza

3:13-17

1:9-11

3:21-38

1:32-34

Chipululu cha Yudeya

Yesu ayesedwa ndi Mdyerekezi

4:1-11

1:12, 13

4:1-13

 

Betaniya wakutsidya lina la Yorodano

Yohane Mʼbatizi ananena kuti Yesu ndi Mwanawankhosa wa Mulungu; ophunzira oyambirira anatsatira Yesu

     

1:15, 29-51

Kana wa ku Galileya; Kaperenao

Chozizwitsa choyamba, madzi anawasandutsa vinyo; anapita ku Kaperenao

     

2:1-12

30, Pasika

Yerusalemu

Anayeretsa kachisi

     

2:13-25

Yesu anakambirana ndi Nikodemo

     

3:1-21

Yudeya; Ainoni

Anapita kumidzi ya ku Yudeya, ophunzira ake anabatiza anthu; Ulaliki womaliza wa Yohane wokhudza Yesu

     

3:22-36

Tiberiyo; Yudeya

Yohane anaikidwa mʼndende; Yesu ananyamuka kupita ku Galileya

4:12; 14:3-5

6:17-20

3:19, 20

4:1-3

Sukari, ku Samariya

Ali pa ulendo wopita ku Galileya, anaphunzitsa Asamariya

     

4:4-43

Chipululu cha Yudeya