Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

A7-C

Zinthu Zikuluzikulu Zimene Yesu Anachita Ali Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu wa Yesu MʼGalileya (Gawo 1)

NTHAWI

MALO

ZIMENE ZINACHITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

30

Galileya

Choyamba Yesu analengeza kuti “Ufumu wakumwamba wayandikira”

4:17

1:14, 15

4:14, 15

4:44, 45

Kana; Nazareti; Kaperenao

Anachiritsa mnyamata; anawerenga mpukutu wa Yesaya; ku Kaperenao

4:13-16

 

4:16-31

4:46-54

Nyanja ya Galileya, pafupi ndi Kaperenao

Anaitana ophunzira 4: Simoni ndi Andireya, Yakobo ndi Yohane

4:18-22

1:16-20

5:1-11

 

Kaperenao

Kuchiritsa apongozi a Simoni ndi ena

8:14-17

1:21-34

4:31-41

 

Galileya

Ulendo woyamba ndi ophunzira 4

4:23-25

1:35-39

4:42, 43

 

Kuchiritsa wakhate; anthu anapita kwa Yesu

8:1-4

1:40-45

5:12-16

 

Kaperenao

Anachiritsa munthu wakufa ziwalo

9:1-8

2:1-12

5:17-26

 

Anaitana Mateyu; anadya ndi okhometsa msonkho; anamufunsa za kusala

9:9-17

2:13-22

5:27-39

 

Yudeya

Analalikira mʼmasunagoge

   

4:44

 

31, Pasika

Yerusalemu

Anachiritsa mwamuna wina ku Betizata; Ayuda ankafuna kumupha

     

5:1-47

Kubwerera kuchokera ku Yerusalemu (?)

Ankabudula ngala za tirigu pa Sabata; Yesu ndi “Mbuye wa Sabata”

12:1-8

2:23-28

6:1-5

 

Galileya; Nyanja ya Galileya

Anachiritsa wolumala pa Sabata; anthu anamutsatira; anachiritsa ena

12:9-21

3:1-12

6:6-11

 

Phiri la ku Kaperenao

Anasankha atumwi 12

 

3:13-19

6:12-16

 

Pafupi ndi Kaperenao

Ulaliki wapaphiri

5:1–7:29

 

6:17-49

 

Kaperenao

Anachiritsa wantchito wa msilikali

8:5-13

 

7:1-10

 

Naini

Anaukitsa mwana wa mkazi wamasiye

   

7:11-17

 

Tiberiyo; Galileya (Naini kapena pafupi)

Yohane anatumiza ophunzira ake kwa Yesu; choonadi chinaululidwa kwa ana aangʼono; goli losavuta kunyamula

11:2-30

 

7:18-35

 

Galileya (Naini kapena pafupi)

Mzimayi wochimwa anathira mafuta pamapazi ake; fanizo la angongole

   

7:36-50

 

Galileya

Ulendo wachiwiri wokalalikira

   

8:1-3

 

Anatulutsa ziwanda; tchimo losakhululukidwa

12:22-37

3:19-30

   

Anapereka chizindikiro cha Yona

12:38-45

     

Kunabwera mayi ndi azichimwene ake; anati abale ake ndi ophunzira ake

12:46-50

3:31-35

8:19-21