Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

A7-E

Zinthu Zikuluzikulu Zimene Yesu Anachita Ali Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu wa Yesu MʼGalileya (Gawo 3) Komanso ku Yudeya

NTHAWI

MALO

ZIMENE ZINACHITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

32, pambuyo pa Pasika

Nyanja ya Galileya; Betsaida

Ali mʼngalawa popita ku Betsaida, Yesu anachenjeza za chofufumitsa cha Afarisi; anachiritsa wosaona

16:5-12

8:13-26

   

Ku Kaisareya wa Filipi

Makiyi a Ufumu; aneneratu za imfa yake ndi kuukitsidwa

16:13-28

8:27–9:1

9:18-27

 

Paphiri la Herimoni

Anasandulika; Yehova analankhula

17:1-13

9:2-13

9:28-36

 

Ku Kaisareya wa Filipi

Anachiritsa mnyamata wogwidwa ndi ziwanda

17:14-20

9:14-29

9:37-43

 

Galileya

Aneneratunso za imfa yake

17:22, 23

9:30-32

9:43-45

 

Kaperenao

Anapereka ndalama ya msonkho

17:24-27

     

Wamkulu kwambiri mu Ufumu; fanizo la nkhosa yosochera ndi la kapolo wosakhululuka

18:1-35

9:33-50

9:46-50

 

Galileya-Samariya

Akupita ku Yerusalemu, anauza ophunzira kuika patsogolo Ufumu

8:19-22

 

9:51-62

7:2-10

Utumiki Womaliza Umene Yesu Anachita ku Yudeya

NTHAWI

MALO

ZIMENE ZINACHITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

32, Chikondwerero cha Misasa (kapena kuti, Mahema)

Yerusalemu

Anaphunzitsa pa Chikondwerero; asilikali anatumidwa kukamanga Yesu

     

7:11-52

Anati “Ine ndine kuwala kwa dziko”; anachiritsa munthu wosaona

     

8:12–9:41

Mwina ku Yudeya

Anatumiza ophunzira 70 kukalalikira

   

10:1-24

 

Yudeya; Betaniya

Fanizo la Msamariya wachifundo; anapita kwa Mariya ndi Marita

   

10:25-42

 

Mwina ku Yudeya

Pemphero lachitsanzo; fanizo lokhudza kulimbikira kupemphera

   

11:1-13

 

Anatulutsa ziwanda; anaperekanso chizindikiro cha Yona

   

11:14-36

 

Anadya ndi Mfarisi; anadzudzula chinyengo cha Afarisi

   

11:37-54

 

Mafanizo: wolemera wopanda nzeru komanso mtumiki wokhulupirika

   

12:1-59

 

Anachiritsa mzimayi wopindika msana pa Sabata; fanizo la kanjere ka mpiru ndi la zofufumitsa

   

13:1-21

 

32, Kupereka Kachisi

Yerusalemu

Fanizo la mʼbusa wabwino; Ayuda ankafuna kumugenda; anapita ku Betaniya wakutsidya la Yorodano

     

10:1-39