Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mabuku a MʼBaibulo

Mabuku a Malemba a Chiheberi, Chikhristu Chisanayambe

DZINA LA BUKU

WOLEMBA

KUMENE ANALEMBERA

NTHAWI IMENE ANAMALIZA KULEMBA (B.C.E.)

NTHAWI YA ZOCHITIKAZO (B.C.E.)

Genesis

Mose

Mʼchipululu

1513

“Pachiyambi” mpaka 1657

Ekisodo

Mose

Mʼchipululu

1512

1657-1512

Levitiko

Mose

Mʼchipululu

1512

Mwezi umodzi (1512)

Numeri

Mose

Mʼchipululu ndi Mʼchigwa cha Mowabu

1473

1512-1473

Deuteronomo

Mose

Mʼchigwa cha Mowabu

1473

Miyezi iwiri (1473)

Yoswa

Yoswa

Kanani

c. 1450

1473–c. 1450

Oweruza

Samueli

Isiraeli

c. 1100

c. 1450–c. 1120

Rute

Samueli

Isiraeli

c. 1090

Zaka 11 za ulamuliro wa Oweruza

1 Samueli

Samueli; Gadi; Natani

Isiraeli

c. 1078

c. 1180-1078

2 Samueli

Gadi; Natani

Isiraeli

c. 1040

1077–c. 1040

1 Mafumu

Yeremiya

Yuda ndi Iguputo

580

c. 1040-911

2 Mafumu

Yeremiya

Yuda ndi Iguputo

580

c. 920-580

1 Mbiri

Ezara

Yerusalemu (?)

c. 460

Kuchokera pa 1 Mbiri 9:44: c. 1077-1037

2 Mbiri

Ezara

Yerusalemu (?)

c. 460

c. 1037-537

Ezara

Ezara

Yerusalemu

c. 460

537–c. 467

Nehemiya

Nehemiya

Yerusalemu

p. 443

456–p. 443

Esitere

Moredikayi

Susani, Elamu

c. 475

493–c. 475

Yobu

Mose

Mʼchipululu

c. 1473

Zaka zoposa 140 kuchokera 1657-1473

Masalimo

Davide ndi ena

 

c. 460

 

Miyambo

Solomo; Aguri; Lemueli

Yerusalemu

c. 717

 

Mlaliki

Solomo

Yerusalemu

i. 1000

 

Nyimbo ya Solomo

Solomo

Yerusalemu

c. 1020

 

Yesaya

Yesaya

Yerusalemu

p. 732

c. 778–p. 732

Yeremiya

Yeremiya

Yuda; Iguputo

580

647-580

Maliro

Yeremiya

Cha ku Yerusalemu

607

 

Ezekieli

Ezekieli

Babulo

c. 591

613–c. 591

Danieli

Danieli

Babulo

c. 536

618–c. 536

Hoseya

Hoseya

Samariya (Chigawo)

p. 745

i. 804–p. 745

Yoweli

Yoweli

Yuda

c. 820 (?)

 

Amosi

Amosi

Yuda

c. 804

 

Obadiya

Obadiya

 

c. 607

 

Yona

Yona

 

c. 844

 

Mika

Mika

Yuda

i. 717

c. 777-717

Nahumu

Nahumu

Yuda

i. 632

 

Habakuku

Habakuku

Yuda

c. 628 (?)

 

Zefaniya

Zefaniya

Yuda

i. 648

 

Hagai

Hagai

Yerusalemu

520

Masiku 112 (520)

Zekariya

Zekariya

Yerusalemu

518

520-518

Malaki

Malaki

Yerusalemu

p. 443

 

Mabuku a Malemba a Chigiriki Olembedwa mu Nthawi ya Chikhristu

DZINA LA BUKU

WOLEMBA

KUMENE ANALEMBERA

NTHAWI IMENE ANAMALIZA KULEMBA (C.E.)

NTHAWI YA ZOCHITIKAZO

Mateyu

Mateyu

Isiraeli

c. 41

2 B.C.E.–33 C.E.

Maliko

Maliko

Roma

c. 60-65

29-33 C.E.

Luka

Luka

Kaisareya

c. 56-58

3 B.C.E.–33 C.E.

Yohane

Mtumwi Yohane

Efeso, kapena chapafupi

c. 98

Pambuyo pa mawu oyamba, 29-33 C.E.

Machitidwe

Luka

Roma

c. 61

33–c. 61 C.E.

Aroma

Paulo

Korinto

c. 56

 

1 Akorinto

Paulo

Efeso

c. 55

 

2 Akorinto

Paulo

Makedoniya

c. 55

 

Agalatiya

Paulo

Korinto kapena Antiokeya wa ku Siriya

c. 50-52

 

Aefeso

Paulo

Roma

c. 60-61

 

Afilipi

Paulo

Roma

c. 60-61

 

Akolose

Paulo

Roma

c. 60-61

 

1 Atesalonika

Paulo

Korinto

c. 50

 

2 Atesalonika

Paulo

Korinto

c. 51

 

1 Timoteyo

Paulo

Makedoniya

c. 61-64

 

2 Timoteyo

Paulo

Roma

c. 65

 

Tito

Paulo

Makedoniya (?)

c. 61-64

 

Filimoni

Paulo

Roma

c. 60-61

 

Aheberi

Paulo

Roma

c. 61

 

Yakobo

Yakobo (mʼbale wa Yesu)

Yerusalemu

i. 62

 

1 Petulo

Petulo

Babulo

c. 62-64

 

2 Petulo

Petulo

Babulo (?)

c. 64

 

1 Yohane

Mtumwi Yohane

Efeso, kapena chapafupi

c. 98

 

2 Yohane

Mtumwi Yohane

Efeso, kapena chapafupi

c. 98

 

3 Yohane

Mtumwi Yohane

Efeso, kapena chapafupi

c. 98

 

Yuda

Yuda (mʼbale wa Yesu)

Isiraeli (?)

c. 65

 

Chivumbulutso

Mtumwi Yohane

Patimo

c. 96

 

[Mayina a anthu omwe analemba mabuku ena ndi malo amene analembera sakudziwika bwinobwino. Madeti ambiri ndi osatsimikizika. Chizindikiro cha “p.” chikutanthauza “pambuyo pa,” chizindikiro cha “i.” chikutanthauza “isanafike” ndipo cha “c.” chikutanthauza “cha mʼma.”]