Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

B14-B

Ndalama ndi Kulemera kwa Zinthu

Ndalama ndi Kulemera kwa Zinthu MʼMalemba a Chiheberi

Gera (1⁄20 ya sekeli)

Magalamu 0.57

Magera 10 = Beka imodzi

Beka

Magalamu 5.7

Mabeka awiri = Sekeli imodzi

Pimu

Magalamu 7.8

Pimu imodzi = 2⁄3 ya sekeli

Kulemera kwa sekeli

Sekeli

Magalamu 11.4

Masekeli 50 = Mina imodzi

Mina

Magalamu 570

Ma mina 60 = Talente imodzi

Talente

Makilogalamu 34.2

Dariki (ya ku Perisiya, yagolide)

Magalamu 8.4

Ezara 8:27

Ndalama ndi Kulemera kwa Zinthu MʼMalemba a Chigiriki

Leputoni (ya Ayuda, yamkuwa)

1⁄2 ya kwadiransi

Luka 21:2

Kwadiransi (ya Aroma, yamkuwa)

Maleputa awiri

Mateyu 5:26

Asariyoni (ya Aroma ndi madera ozungulira, yamkuwa)

Makwadiransi 4

Mateyu 10:29

Dinari (ya Aroma, yasiliva)

Makwadiransi 64 Magalamu 3.85

Mateyu 20:10

Malipiro a Tsiku Limodzi (Maola 12)

Malipiro a Masiku Awiri

Dalakima (ya Agiriki, yasiliva)

Magalamu 3.4

Luka 15:8

Malipiro a Tsiku Limodzi (Maola 12)

Didalakima (ya Agiriki, yasiliva)

Madalakima awiri

Magalamu 6.8

Mateyu 17:24

Malipiro a Masiku Atatu

Tetiradalakima ya ku Antiokeya

Tetiradalakima ya ku Turo (Sekeli yasiliva ya ku Turo)

Tetiradalakima (ya Agiriki, yasiliva; imatchedwanso siteta yasiliva)

Madalakima 4

Magalamu 13.6

Mateyu 17:27

Malipiro a Masiku 4

Mina

Madalakima 100

Magalamu 340

Luka 19:13

= Malipiro a masiku pafupifupi 100

Talente

Ma mina 60

Makilogalamu 20.4

Mateyu 18:24

Chivumbulutso 16:21

= Malipiro a zaka pafupifupi 20

Paundi (ya Aroma)

Magalamu 327

Yohane 12:3

‘Mafuta okwana magalamu 327, nado weniweniʼ