Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

A7-F

Zinthu Zikuluzikulu Zimene Yesu Anachita Ali Padziko Lapansi—Utumiki Womaliza Umene Yesu Anachita Kumʼmawa kwa Yorodano

NTHAWI

MALO

ZIMENE ZINACHITIKA

MATEYU

MALIKO

LUKA

YOHANE

32, pambuyo pa Chikondwerero Chopereka Kachisi kwa Mulungu

Betaniya wakutsidya kwa Yorodano

Anapita kumene Yohane ankabatizira; ambiri anakhulupirira Yesu

     

10:40-42

Pereya

Anaphunzitsa mʼmizinda ndi mʼmidzi, akulowera ku Yerusalemu

   

13:22

 

Anawauza kuti alowe pakhomo lalingʼono; anadandaulira Yerusalemu

   

13:23-35

 

Mwina ku Pereya

Anaphunzitsa za kudzichepetsa; mafanizo: malo olemekezeka komanso alendo amene sanabwere kuphwando

   

14:1-24

 

Udindo wokhala wophunzira

   

14:25-35

 

Mafanizo: nkhosa yosowa, ndalama yotaika, mwana wolowerera

   

15:1-32

 

Mafanizo: mtumiki wosalungama, munthu wolemera ndi Lazaro

   

16:1-31

 

Anaphunzitsa za kukhumudwitsana, kukhululukirana ndi chikhulupiriro

   

17:1-10

 

Betaniya

Lazaro anamwalira ndi kuukitsidwa

     

11:1-46

Yerusalemu; Efuraimu

Chiwembu chopha Yesu; anachokako

     

11:47-54

Samariya; Galileya

Anachiritsa akhate 10; anaphunzitsa za kubwera kwa Ufumu wa Mulungu

   

17:11-37

 

Samariya kapena Galileya

Mafanizo: mkazi wamasiye wakhama, Mfarisi ndi wokhometsa msonkho

   

18:1-14

 

Pereya

Anaphunzitsa zokhudza ukwati

19:1-12

10:1-12

   

Anadalitsa ana

19:13-15

10:13-16

18:15-17

 

Funso la munthu wolemera; fanizo la antchito amʼmunda wa mpesa ndi malipiro ofanana

19:16–20:16

10:17-31

18:18-30

 

Mwina ku Pereya

Kachitatu ananeneratu za imfa yake

20:17-19

10:32-34

18:31-34

 

Yakobo ndi Yohane anapempha malo mu Ufumu

20:20-28

10:35-45

   

Yeriko

Podutsa, anachiritsa amuna awiri osaona; anapita kwa Zakeyu; fanizo la ndalama zokwana ma mina 10

20:29-34

10:46-52

18:35–19:28