Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

A6-B

Tchati: Aneneri Komanso Mafumu a Yuda ndi Isiraeli (Gawo 2)

Mafumu a mu Ufumu Wakumʼmwera (Kupitiriza)

777 B.C.E.

Yotamu: zaka 16

762

Ahazi: zaka 16

746

Hezekiya: zaka 29

716

Manase: zaka 55

661

Amoni: zaka ziwiri

659

Yosiya: zaka 31

628

Yehoahazi: miyezi itatu

Yehoyakimu: zaka 11

618

Yehoyakini: miyezi itatu ndi masiku 10

617

Zedekiya: zaka 11

607

Magulu ankhondo a ku Babulo anawononga Yerusalemu ndi kachisi wake motsogoleredwa ndi Nebukadinezara. Zedekiya, mfumu yomaliza yochokera mumzere wa Davide, inachotsedwa pampando

Mafumu a mu Ufumu Wakumpoto (Kupitiriza)

c. 803 B.C.E.

Zekariya: analamulira kwa miyezi 6 yokha

Tinganene kuti Zekariya anayamba kulamulira, koma zinali zisanatsimikizirike kuti ufumuwo ndi wake mpaka cha mʼma 792

c. 791

Salumu: mwezi umodzi

Menahemu: zaka 10

c. 780

Pekahiya: zaka ziwiri

c. 778

Peka: zaka 20

c. 758

Hoshiya: zaka 9 kuchokera cha mʼma 748

c. 748

Zikuoneka kuti ufumu wa Hoshiya unakhazikika kapena nʼkutheka kuti ankathandizidwa ndi mfumu ya Asuri dzina lake Tigilati-pilesere Wachitatu cha mʼma 748

740

Asuri analanda Samariya, nʼkuyamba kulamulira Aisiraeli; ufumu wa mafuko 10 wa Isiraeli unatha

  • Mayina a Aneneri

  • Yesaya

  • Mika

  • Zefaniya

  • Yeremiya

  • Nahumu

  • Habakuku

  • Danieli

  • Ezekieli

  • Obadiya

  • Hoseya