Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

B5

Chihema Chopatulika Komanso Mkulu wa Ansembe

Mbali za Chihema Chopatulika

  1. 1 Likasa (Eks. 25:10-22; 26:33)

  2. 2 Katani (Eks. 26:31-33)

  3. 3 Chipilala Chopachikapo Katani (Eks. 26:31, 32)

  4. 4 Malo Oyera (Eks. 26:33)

  5. 5 Malo Oyera Koposa (Eks. 26:33)

  6. 6 Nsalu Yotchinga Khomo la Chihema (Eks. 26:36)

  7. 7 Chipilala Chopachikapo Nsalu Yotchinga Khomo (Eks. 26:37)

  8. 8 Zitsulo Zakopa Zokhazikapo Zipilala (Eks. 26:37)

  9. 9 Guwa Lansembe Zofukiza (Eks. 30:1-6)

  10. 10 Tebulo la Mkate Wachionetsero (Eks. 25:23-30; 26:35)

  11. 11 Choikapo Nyale (Eks. 25:31-40; 26:35)

  12. 12 Nsalu ya Tenti (Eks. 26:1-6)

  13. 13 Nsalu ya Tenti ya Ubweya wa Mbuzi (Eks. 26:7-13)

  14. 14 Zikopa za Nkhosa Zophimbira (Eks. 26:14)

  15. 15 Zikopa za Akatumbu Zophimbira (Eks. 26:14)

  16. 16 Mafelemu Oimika (Eks. 26:15-18, 29)

  17. 17 Zitsulo Zasiliva Zokhazikapo Mafelemu Oimika (Eks. 26:19-21)

  18. 18 Ndodo (Eks. 26:26-29)

  19. 19 Zitsulo Zasiliva (Eks. 26:32)

  20. 20 Beseni Losambira Lakopa (Eks. 30:18-21)

  21. 21 Guwa Lansembe Zopsereza (Eks. 27:1-8)

  22. 22 Bwalo (Eks. 27:17, 18)

  23. 23 Khomo la Bwalo (Eks. 27:16)

  24. 24 Nsalu Zotchingira Mpanda (Eks. 27:9-15)

Mkulu wa Ansembe

Chaputala 28 cha buku la Ekisodo chimafotokoza mwatsatanetsatane zovala za mkulu wa ansembe wa Isiraeli