Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la Ekisodo

Machaputala

Mitu

  • 1

    • Aisiraeli anachulukana ku Iguputo (1-7)

    • Farao anazunza Aisiraeli (8-14)

    • Azamba oopa Mulungu anapulumutsa ana (15-22)

  • 2

    • Kubadwa kwa Mose (1-4)

    • Mwana wamkazi wa Farao anatenga Mose kuti akhale mwana wake (5-10)

    • Mose anathawira ku Midiyani ndipo anakwatira Zipora (11-22)

    • Mulungu anamva kulira kwa Aisiraeli (23-25)

  • 3

    • Mose komanso chitsamba chaminga choyaka moto (1-12)

    • Yehova anafotokoza za dzina lake (13-15)

    • Yehova anapatsa Mose malangizo (16-22)

  • 4

    • Zizindikiro zitatu zimene Mose anachita (1-9)

    • Mose ankadziona kuti sangakwanitse ntchito imene Mulungu anamupatsa (10-17)

    • Mose anabwerera ku Iguputo (18-26)

    • Mose anakumananso ndi Aroni (27-31)

  • 5

    • Mose ndi Aroni anapita kwa Farao (1-5)

    • Aisiraeli anapitiriza kuzunzidwa kwambiri (6-18)

    • Aisiraeli anayamba kuimba mlandu Mose komanso Aroni (19-23)

  • 6

    • Anawauzanso lonjezo lakuti adzawalanditsa ku ukapolo (1-13)

      • Dzina la Yehova silinadziwike mokwanira (2, 3)

    • Mzere wobadwira wa Mose ndi Aroni (14-27)

    • Mose anakaonekeranso pamaso pa Farao (28-30)

  • 7

    • Yehova analimbikitsa Mose (1-7)

    • Ndodo ya Aroni inasanduka njoka yaikulu (8-13)

    • Mliri woyamba: madzi anasanduka magazi (14-25)

  • 8

    • Mliri wachiwiri: achule (1-15)

    • Mliri wachitatu: tizilombo touluka toyamwa magazi (16-19)

    • Mliri wa 4: ntchentche zoluma (20-32)

      • Dera la Goseni silinakhudzidwe (22, 23)

  • 9

    • Mliri wa 5: kufa kwa ziweto (1-7)

    • Mliri wa 6: zithupsa pa anthu ndi nyama (8-12)

    • Mliri wa 7: mvula ya matalala (13-35)

      • Farao anaona mphamvu za Mulungu (16)

      • Dzina la Yehova linalengezedwa (16)

  • 10

    • Mliri wa 8: dzombe (1-20)

    • Mliri wa 9: mdima (21-29)

  • 11

    • Ananena za mliri wa 10 (1-10)

      • Aisiraeli anapempha mphatso (2)

  • 12

    • Kukhazikitsidwa kwa Pasika (1-28)

      • Magazi anawazidwa pazitseko (7)

    • Mliri wa 10: ana oyamba kubadwa anaphedwa (29-32)

    • Aisiraeli anachoka ku Iguputo (33-42)

      • Kutha kwa zaka 430 (40, 41)

    • Malangizo okhudza kuchita nawo Pasika (43-51)

  • 13

    • Mwana wamwamuna woyamba kubadwa aliyense ndi wa Yehova (1, 2)

    • Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa (3-10)

    • Mwana wamwamuna woyamba kubadwa aliyense ankaperekedwa kwa Mulungu (11-16)

    • Aisiraeli anatsogoleredwa kupita ku Nyanja Yofiira (17-20)

    • Chipilala cha mtambo komanso cha moto (21, 22)

  • 14

    • Aisiraeli anafika panyanja (1-4)

    • Farao analondola Aisiraeli (5-14)

    • Aisiraeli anaoloka Nyanja Yofiira (15-25)

    • Aiguputo anamira mʼnyanja (26-28)

    • Aisiraeli anakhulupirira Yehova (29-31)

  • 15

    • Mose ndi Aisiraeli anaimba nyimbo yosonyeza kupambana (1-19)

    • Miriamu anathirira mangʼombe (20, 21)

    • Madzi owawa anakhala okoma (22-27)

  • 16

    • Anthu anangʼungʼudza zokhudza chakudya (1-3)

    • Yehova anamva kungʼungʼudza kwa anthu (4-12)

    • Anapatsidwa zinziri ndi mana (13-21)

    • Mana sankapezeka tsiku la Sabata (22-30)

    • Anasunga mana kuti chikhale chikumbutso (31-36)

  • 17

    • Anadandaula za kusowa kwa madzi ku Horebu (1-4)

    • Madzi anatuluka kuchokera mʼthanthwe (5-7)

    • Aamaleki anakaukira Aisiraeli koma anagonjetsedwa (8-16)

  • 18

    • Kufika kwa Yetero ndi Zipora (1-12)

    • Yetero anapatsa Mose malangizo oti asankhe oweruza (13-27)

  • 19

    • Paphiri la Sinai (1-25)

      • Isiraeli adzakhala ufumu wa ansembe (5, 6)

      • Anthu anayeretsedwa kuti akumane ndi Mulungu (14, 15)

  • 20

    • Malamulo Khumi (1-17)

    • Aisiraeli anachita mantha chifukwa cha zimene ankamva ndi kuona (18-21)

    • Malangizo okhudza kulambira (22-26)

  • 21

    • Zigamulo zoti Aisiraeli azitsatira (1-36)

      • Zokhudza akapolo a Chiheberi (2-11)

      • Zokhudza nkhanza zochitidwa kwa munthu (12-27)

      • Zokhudza nyama (28-36)

  • 22

    • Zigamulo zoti Aisiraeli azitsatira (1-31)

      • Zokhudza kuba (1-4)

      • Zokhudza kuonongeka kwa mbewu (5, 6)

      • Zokhudza kulipira zinthu ndi katundu wamwini (7-15)

      • Zokhudza kunyengerera mkazi (16, 17)

      • Zokhudza kulambira komanso chilungamo (18-31)

  • 23

    • Zigamulo zoti Aisiraeli azitsatira (1-19)

      • Zokhudza kuona mtima komanso kuchita zinthu mwachilungamo (1-9)

      • Zokhudza masabata ndi zikondwerero (10-19)

    • Mngelo anatsogolera Aisiraeli (20-26)

    • Kutenga dziko komanso malire ake (27-33)

  • 24

    • Anthu anavomereza kuti adzasunga pangano (1-11)

    • Mose paphiri la Sinai (12-18)

  • 25

  • 26

    • Chihema (1-37)

      • Nsalu za tenti (1-14)

      • Mafelemu ndi zoikapo mafelemu (15-30)

      • Katani ndi nsalu yotchinga (31-37)

  • 27

    • Guwa la nsembe zopsereza (1-8)

    • Bwalo (9-19)

    • Mafuta a nyale (20, 21)

  • 28

    • Zovala za ansembe (1-5)

    • Efodi (6-14)

    • Chovala pachifuwa (15-30)

      • Urimu ndi Tumimu (30)

    • Malaya odula manja (31-35)

    • Nduwira ndi kachitsulo kagolide (36-39)

    • Zovala zina za ansembe (40-43)

  • 29

    • Kuikidwa kwa ansembe (1-37)

    • Nsembe ya tsiku ndi tsiku (38-46)

  • 30

    • Guwa la nsembe zofukiza (1-10)

    • Kalembera komanso ndalama zophimbira machimo (11-16)

    • Beseni losambira lakopa (17-21)

    • Mafuta odzozera osakanizidwa mwapadera (22-33)

    • Kapangidwe ka zofukiza zopatulika (34-38)

  • 31

    • Mulungu anapereka mzimu wake kwa anthu aluso (1-11)

    • Sabata linali chizindikiro pakati pa Mulungu ndi Aisiraeli (12-17)

    • Miyala iwiri yosema (18)

  • 32

    • Kulambira mwana wangʼombe wagolide (1-35)

      • Mose anamva kuimba kwa mtundu wina (17, 18)

      • Mose anaphwanya miyala imene analembapo malamulo (19)

      • Alevi anakhala okhulupirika kwa Yehova (26-29)

  • 33

    • Uthenga wa Mulungu wowadzudzula (1-6)

    • Chihema chokumanako kunja kwa msasa (7-11)

    • Mose anapempha kuti aone ulemerero wa Yehova (12-23)

  • 34

    • Anapanganso miyala ina yosema (1-4)

    • Mose anaona ulemerero wa Yehova (5-9)

    • Mfundo zokhudza pangano zinabwerezedwa (10-28)

    • Nkhope ya Mose inkawala (29-35)

  • 35

    • Malangizo okhudza Sabata (1-3)

    • Zopereka za chihema (4-29)

    • Bezaleli komanso Oholiabu anapatsidwa mzimu wa Mulungu (30-35)

  • 36

    • Anabweretsa zopereka zochuluka kuposa zimene zinkafunika (1-7)

    • Kumangidwa kwa chihema (8-38)

  • 37

    • Kupanga Likasa (1-9)

    • Tebulo (10-16)

    • Choikapo nyale (17-24)

    • Guwa la nsembe zofukiza (25-29)

  • 38

    • Guwa la nsembe zopsereza (1-7)

    • Beseni lakopa (8)

    • Bwalo (9-20)

    • Kuwerengera zinthu zimene anagwiritsa ntchito popanga chihema (21-31)

  • 39

    • Kupanga zovala za ansembe (1)

    • Efodi (2-7)

    • Chovala pachifuwa (8-21)

    • Malaya odula manja (22-26)

    • Zovala zina za ansembe (27-29)

    • Kachitsulo kagolide (30, 31)

    • Mose anayendera chihema (32-43)

  • 40

    • Kumanga chihema (1-33)

    • Ulemerero wa Yehova unadzaza mʼchihema (34-38)