Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kalata Yopita kwa Akolose

Machaputala

1 2 3 4

Mitu

  • 1

    • Moni (1, 2)

    • Kuthokoza chifukwa cha chikhulupiriro cha Akolose (3-8)

    • Kuwapempherera kuti akule mwauzimu (9-12)

    • Udindo waukulu wa Khristu (13-23)

    • Paulo anagwira ntchito mwakhama pothandiza mpingo (24-29)

  • 2

    • Chinsinsi chopatulika cha Mulungu, Khristu (1-5)

    • Samalani ndi anthu opusitsa anzawo (6-15)

    • Zenizeni zake zinakwaniritsidwa ndi Khristu (16-23)

  • 3

    • Umunthu wakale komanso watsopano (1-17)

      • Chititsani ziwalo za thupi lanu kukhala zakufa (5)

      • Chikondi chimagwirizanitsa anthu mwamphamvu kwambiri kuposa chinthu china chilichonse (14)

    • Malangizo opita ku mabanja a Chikhristu (18-25)

  • 4

    • Malangizo opita kwa ambuye (1)

    • “Muzilimbikira kupemphera” (2-4)

    • Kuchita zinthu mwanzeru pokhala ndi anthu akunja (5, 6)

    • Moni womaliza (7-18)