Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kalata Yopita Kwa Agalatiya

Machaputala

1 2 3 4 5 6

Mitu

  • 1

    • Moni (1-5)

    • Palibe uthenga wina wabwino (6-9)

    • Uthenga wabwino umene Paulo ankalalikira ndi wochokera kwa Mulungu (10-12)

    • Kutembenuka kwa Paulo komanso zimene ankachita poyamba (13-24)

  • 2

    • Paulo anakumana ndi atumwi ku Yerusalemu (1-10)

    • Paulo anadzudzula Petulo (Kefa) (11-14)

    • Munthu amayesedwa wolungama chifukwa cha chikhulupiriro (15-21)

  • 3

    • Ntchito za Chilamulo komanso chikhulupiriro (1-14)

      • Wolungama adzakhala ndi moyo chifukwa cha chikhulupiriro (11)

    • Lonjezo la Abulahamu silinkadalira Chilamulo (15-18)

      • Khristu ndi mbadwa ya Abulahamu (16)

    • Kumene Chilamulo chinachokera komanso cholinga chake (19-25)

    • Ndinu ana a Mulungu chifukwa cha chikhulupiriro (26-29)

      • Ophunzira a Khristu ndi mbadwa za Abulahamu (29)

  • 4

    • Si inunso akapolo koma ana (1-7)

    • Paulo ankadera nkhawa Agalatiya (8-20)

    • Hagara ndi Sara: mapangano awiri (21-31)

      • Yerusalemu wamʼmwamba ndi mfulu ndipo ndi mayi athu (26)

  • 5

    • Ufulu wa Akhristu (1-15)

    • Kuyenda motsogoleredwa ndi mzimu (16-26)

      • Ntchito za thupi (19-21)

      • Makhalidwe amene anthu amakhala nawo mothandizidwa ndi mzimu woyera (22, 23)

  • 6

    • Muzinyamulirana zinthu zolemera (1-10)

      • Timakolola zimene tafesa (7, 8)

    • Mdulidwe wopanda phindu (11-16)

      • Kulengedwa mwatsopano (15)

    • Mawu omaliza (17, 18)