Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kalata Yachiwiri ya Petulo

Machaputala

1 2 3

Mitu

  • 1

    • Moni (1)

    • Mupitirizebe kukhala pakati pa anthu oitanidwa (2-15)

      • Makhalidwe ofunika kuwonjezera pa chikhulupiriro (5-9)

    • Mawu aulosi adzakwaniritsidwa (16-21)

  • 2

    • Kudzakhala aphunzitsi abodza (1-3)

    • Umboni wotsimikizira kuti aphunzitsi abodza adzaweruzidwa (4-10a)

      • Angelo anawaponya mu Tatalasi (4)

      • Chigumula; Sodomu ndi Gomora (5-7)

    • Mmene tingadziwire aphunzitsi abodza (10b-22)

  • 3

    • Anthu onyoza amakayikira zoti anthu oipa adzawonongedwa (1-7)

    • Yehova sakuchedwa (8-10)

    • Ganizirani za mtundu wa anthu amene muyenera kukhala (11-16)

      • Kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano (13)

    • Chenjerani kuti anthu asakusocheretseni (17, 18)