Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kalata Yachiwiri Yopita kwa Akorinto

Machaputala

1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 11 12 13

Mitu

  • 1

    • Mawu oyamba (1, 2)

    • Mulungu amatitonthoza pa vuto lililonse (3-11)

    • Paulo anasintha mapulani a ulendo wake (12-24)

  • 2

    • Paulo ankafuna kuti Akhristu a ku Korinto asangalale (1-4)

    • Wochimwa anakhululukidwa nʼkubwezeretsedwa (5-11)

    • Paulo anapita ku Torowa ndiponso ku Makedoniya (12, 13)

    • Utumiki, kuguba ponyadira kupambana (14-17)

      • Sitichita malonda ndi mawu a Mulungu (17)

  • 3

    • Makalata otichitira umboni (1-3)

    • Atumiki a pangano latsopano (4-6)

    • Ulemerero wa pangano latsopano ndi waukulu (7-18)

  • 4

    • Kuwala kwa uthenga wabwino (1-6)

      • Maganizo a osakhulupirira anachititsidwa khungu (4)

    • Chuma mʼzonyamulira zadothi (7-18)

  • 5

    • Kuvala nyumba ya kumwamba (1-10)

    • Utumiki wogwirizanitsa anthu ndi Mulungu (11-21)

      • Cholengedwa chatsopano (17)

      • Akazembe mʼmalo mwa Khristu (20)

  • 6

    • Osagwiritsa ntchito molakwa kukoma mtima kwa Mulungu (1, 2)

    • Utumiki wa Paulo (3-13)

    • Musamangidwe mʼgoli ndi osakhulupirira (14-18)

  • 7

    • Tidziyeretse kuchotsa choipitsa chilichonse (1)

    • Paulo anasangalala ndi Akorinto (2-4)

    • Tito anabwera ndi lipoti labwino (5-7)

    • Chisoni chogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu ndiponso kulapa (8-16)

  • 8

    • Zopereka za Akhristu a ku Yudeya (1-15)

    • Tito anatumizidwa ku Korinto (16-24)

  • 9

    • Analimbikitsidwa kukhala opatsa (1-15)

      • Mulungu amakonda wopereka mosangalala (7)

  • 10

    • Paulo anafotokoza zokhudza utumiki wake (1-18)

      • Zida zankhondo yathu si zochokera mʼdziko (4, 5)

  • 11

    • Paulo ndiponso atumwi apamwamba (1-15)

    • Mavuto amene mtumwi Paulo anakumana nawo (16-33)

  • 12

    • Masomphenya a Paulo (1-7a)

    • “Minga mʼthupi” la Paulo (7b-10)

    • Sankachepa poyerekezera ndi atumwi apamwamba (11-13)

    • Paulo ankadera nkhawa Akorinto (14-21)

  • 13

    • Malangizo komanso machenjezo omaliza (1-14)

      • “Pitirizani kudziyesa kuti muone ngati mukadali ndi chikhulupiriro” (5)

      • Kusintha maganizo; kukhala ndi maganizo ogwirizana (11)