Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la Yoswa

Machaputala

Mitu

  • 1

    • Yehova analimbikitsa Yoswa (1-9)

      • Kuwerenga Chilamulo ndi kuganizira mozama (8)

    • Kukonzekera kuwoloka Yorodano (10-18)

  • 2

    • Yoswa anatumiza anthu awiri kukafufuza zokhudza Yeriko (1-3)

    • Rahabi anabisa anthu okafufuza (4-7)

    • Analonjeza Rahabi (8-21a)

      • Chizindikiro cha chingwe chofiira (18)

    • Okafufuza zokhudza mzinda anabwerera kwa Yoswa (21b-24)

  • 3

    • Aisiraeli anawoloka Yorodano (1-17)

  • 4

    • Miyala ya chikumbutso (1-24)

  • 5

    • Mdulidwe ku Giligala (1-9)

    • Chikondwerero cha Pasika; mana anasiya (10-12)

    • Kalonga wa gulu lankhondo la ­Yehova (13-15)

  • 6

    • Mpanda wa Yeriko unagwa (1-21)

    • Rahabi ndi banja lake anapulumuka (22-27)

  • 7

    • Aisiraeli anagonjetsedwa ku Ai (1-5)

    • Pemphero la Yoswa (6-9)

    • Aisiraeli anagonjetsedwa chifukwa cha tchimo (10-15)

    • Tchimo la Akani linadziwika, anaponyedwa miyala (16-26)

  • 8

    • Yoswa anatumiza anthu oti akabisalire anthu a ku Ai (1-13)

    • Mzinda wa Ai unagonjetsedwa (14-29)

    • Chilamulo chinawerengedwa paphiri la Ebala (30-35)

  • 9

    • Agibiyoni ochenjera anapempha mgwirizano (1-15)

    • Bodza la Agibiyoni linadziwika (16-21)

    • Agibiyoni anakhala otola nkhuni ndi kutunga madzi (22-27)

  • 10

    • Aisiraeli anathandiza Agibiyoni (1-7)

    • Yehova anamenyera nkhondo Aisiraeli (8-15)

      • Adani amene ankathawa anaphedwa ndi matalala (11)

      • Dzuwa linaima (12-14)

    • Mafumu 5 anaphedwa (16-28)

    • Analanda mizinda yakumʼmwera (29-43)

  • 11

    • Analanda mizinda yakumpoto (1-15)

    • Madera amene Yoswa anagonjetsa (16-23)

  • 12

    • Mafumu amene anagonjetsedwa kumʼmawa kwa Yorodano (1-6)

    • Mafumu amene anagonjetsedwa kumadzulo kwa Yorodano (7-24)

  • 13

    • Madera amene anali asanalandidwe (1-7)

    • Kugawa malo a kumʼmawa kwa Yorodano (8-14)

    • Cholowa cha fuko la Rubeni (15-23)

    • Cholowa cha fuko la Gadi (24-28)

    • Cholowa cha Manase, kumʼmawa kwa Yorodano (29-32)

    • Yehova ndi cholowa cha Alevi (33)

  • 14

    • Kugawa malo kumadzulo kwa Yorodano (1-5)

    • Kalebe anapatsidwa Heburoni kuti akhale cholowa chake (6-15)

  • 15

    • Cholowa cha fuko la Yuda (1-12)

    • Mwana wamkazi wa Kalebe analandira malo (13-19)

    • Mizinda ya anthu a fuko la Yuda (20-63)

  • 16

    • Cholowa cha mbadwa za Yosefe (1-4)

    • Cholowa cha fuko la Efuraimu (5-10)

  • 17

    • Cholowa cha Manase ­chakumadzulo (1-13)

    • Dera lina la mbadwa za Yosefe (14-18)

  • 18

    • Dera lotsala linagawidwa ku Silo (1-10)

    • Cholowa cha fuko la Benjamini (11-28)

  • 19

    • Cholowa cha fuko la Simiyoni (1-9)

    • Cholowa cha fuko la Zebuloni (10-16)

    • Cholowa cha fuko la Isakala (17-23)

    • Cholowa cha fuko la Aseri (24-31)

    • Cholowa cha fuko la Nafitali (32-39)

    • Cholowa cha fuko la Dani (40-48)

    • Cholowa cha Yoswa (49-51)

  • 20

    • Mizinda yothawirako (1-9)

  • 21

    • Mizinda ya Alevi (1-42)

      • Mizinda ya ana a Aroni (9-19)

      • Mizinda ya Akohati otsala (20-26)

      • Mizinda ya Agerisoni (27-33)

      • Mizinda ya Amerari (34-40)

    • Malonjezo a Yehova anakwaniritsidwa (43-45)

  • 22

    • Mafuko akumʼmawa anabwerera kwawo (1-8)

    • Anamanga guwa ku Yorodano (9-12)

    • Anafotokoza cholinga cha guwa (13-29)

    • Anagwirizananso (30-34)

  • 23

    • Yoswa anatsanzikana ndi atsogoleri a Aisiraeli (1-16)

      • Mawu onse a Yehova anakwaniritsidwa (14)

  • 24

    • Yoswa anafotokoza mbiri ya Aisiraeli (1-13)

    • Anawalimbikitsa kutumikira Yehova (14-24)

      • “Ine ndi banja langa tizitumikira Yehova” (15)

    • Yoswa anachita pangano ndi Aisiraeli (25-28)

    • Yoswa anamwalira nʼkuikidwa mʼmanda (29-31)

    • Mafupa a Yosefe anaikidwa mʼmanda ku Sekemu (32)

    • Eliezara anamwalira nʼkuikidwa mʼmanda (33)