Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la Nahumu

Machaputala

1 2 3

Mitu

  • 1

    • Mulungu analanga adani ake (1-7)

      • Mulungu amafuna kuti tizidzipereka kwa iye yekha (2)

      • Yehova amadziwa anthu amene amathawira kwa iye (7)

    • Nineve adzawonongedwa (8-14)

      • Mavuto sadzachitikanso (9)

    • Uthenga wabwino wokhudza Yuda unalengezedwa (15)

  • 2

    • Nineve adzakhala bwinja (1-13)

      • “Zotsekera madzi amʼmitsinje zidzatsegulidwa” (6)

  • 3

    • “Tsoka mzinda wokhetsa magazi” (1-19)

      • Zomwe zidzachititse kuti Nineve awonongedwe (1-7)

      • Nineve adzawonongedwa ngati No-amoni (8-12)

      • Nineve sadzalephera kuwonongedwa (13-19)