Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Uthenga Wabwino Wolembedwa ndi Luka

Machaputala

Mitu

  • 1

    • Kalata yopita kwa a Teofilo (1-4)

    • Gabrieli ananeneratu za kubadwa kwa Yohane Mʼbatizi (5-25)

    • Gabrieli ananeneratu za kubadwa kwa Yesu (26-38)

    • Mariya anapita kwa Elizabeti (39-45)

    • Mariya analemekeza Yehova (46-56)

    • Kubadwa kwa Yohane komanso mmene anamupatsira dzina (57-66)

    • Ulosi wa Zekariya (67-80)

  • 2

    • Kubadwa kwa Yesu (1-7)

    • Angelo anaonekera kwa abusa (8-20)

    • Mdulidwe komanso kuyeretsedwa (21-24)

    • Simiyoni anaona Khristu (25-35)

    • Anna analankhula zokhudza mwanayo (36-38)

    • Anabwerera ku Nazareti (39, 40)

    • Yesu anapita kukachisi ali ndi zaka 12 (41-52)

  • 3

    • Chiyambi cha ntchito ya Yohane (1, 2)

    • Yohane ankalimbikitsa anthu kuti abatizidwe (3-20)

    • Kubatizidwa kwa Yesu (21, 22)

    • Mzere wa makolo a Yesu Khristu (23-38)

  • 4

    • Mdyerekezi anayesa Yesu (1-13)

    • Yesu anayamba kulalikira ku Galileya (14, 15)

    • Yesu anakanidwa ku Nazareti (16-30)

    • Zimene zinachitika musunagoge ku Kaperenao (31-37)

    • Apongozi a Simoni ndi anthu ena anachiritsidwa (38-41)

    • Gulu la anthu linapeza Yesu ali kwayekha (42-44)

  • 5

    • Anagwira nsomba mozizwitsa; ophunzira oyambirira (1-11)

    • Munthu wakhate anachiritsidwa (12-16)

    • Yesu anachiritsa munthu wakufa ziwalo (17-26)

    • Yesu anaitana Levi (27-32)

    • Funso lokhudza kusala kudya (33-39)

  • 6

    • Yesu ndi “Mbuye wa Sabata” (1-5)

    • Munthu wolumala dzanja anachiritsidwa (6-11)

    • Atumwi 12 (12-16)

    • Yesu ankaphunzitsa komanso kuchiritsa anthu (17-19)

    • Anthu osangalala komanso amene ali ndi tsoka (20-26)

    • Kukonda adani (27-36)

    • Siyani kuweruza (37-42)

    • Umadziwika ndi zipatso zake (43-45)

    • Nyumba yomangidwa bwino; nyumba yopanda maziko olimba (46-49)

  • 7

    • Chikhulupiriro cha mtsogoleri wa asilikali (1-10)

    • Yesu anaukitsa mwana wamwamuna wa mkazi wamasiye ku Naini (11-17)

    • Yohane Mʼbatizi anatamandidwa (18-30)

    • Anadzudzula mʼbadwo wosamvera (31-35)

    • Mkazi wochimwa anakhululukidwa (36-50)

      • Fanizo la anthu amene anatenga ngongole (41-43)

  • 8

    • Azimayi ankayenda ndi Yesu (1-3)

    • Fanizo la wofesa mbewu (4-8)

    • Chifukwa chake Yesu ankagwiritsa ntchito mafanizo (9, 10)

    • Anafotokoza tanthauzo la fanizo la wofesa mbewu (11-15)

    • Munthu akayatsa nyale saivundikira (16-18)

    • Amayi ake a Yesu komanso azichimwene ake (19-21)

    • Yesu analetsa mphepo yamphamvu (22-25)

    • Yesu anatumiza ziwanda munkhumba (26-39)

    • Mwana wamkazi wa Yairo; mzimayi anagwira chovala cha Yesu (40-56)

  • 9

    • Atumwi 12 anapatsidwa malangizo okhudza utumiki (1-6)

    • Herode anathedwa nzeru ndi zimene Yesu ankachita (7-9)

    • Yesu anadyetsa anthu 5,000 (10-17)

    • Petulo anazindikira kuti Yesu ndi Khristu (18-20)

    • Yesu ananeneratu za imfa yake (21, 22)

    • Wophunzira weniweni wa Yesu (23-27)

    • Yesu anasintha maonekedwe ake (28-36)

    • Mnyamata wogwidwa ndi chiwanda anachiritsidwa (37-43a)

    • Yesu ananeneratu za imfa yake kachiwiri (43b-45)

    • Ophunzira anakangana kuti wamkulu ndi ndani (46-48)

    • Amene sakutsutsana nafe ali kumbali yathu (49, 50)

    • Mudzi wa Asamariya unakana Yesu (51-56)

    • Zimene munthu angachite kuti akhale wotsatira wa Yesu (57-62)

  • 10

    • Yesu anatumiza ophunzira 70 (1-12)

    • Tsoka mizinda yosalapa (13-16)

    • Ophunzira 70 aja anabwerera (17-20)

    • Yesu anatamanda Atate wake chifukwa chokomera mtima anthu odzichepetsa (21-24)

    • Fanizo la Msamariya wachifundo (25-37)

    • Yesu anapita kwa Marita ndi Mariya (38-42)

  • 11

    • Mmene tingapempherere (1-13)

      • Pemphero lachitsanzo (2-4)

    • Ankatulutsa ziwanda ndi chala cha Mulungu (14-23)

    • Mizimu yonyansa inabwerera (24-26)

    • Kusangalala kwenikweni (27, 28)

    • Chizindikiro cha Yona (29-32)

    • Nyale ya thupi (33-36)

    • Tsoka kwa atsogoleri achipembedzo achinyengo (37-54)

  • 12

    • Zofufumitsa za Afarisi (1-3)

    • Muziopa Mulungu, osati anthu (4-7)

    • Kuvomereza kuti ndife ophunzira a Khristu (8-12)

    • Fanizo la munthu wolemera koma wopusa (13-21)

    • Siyani kuda nkhawa (22-34)

      • Kagulu ka nkhosa (32)

    • Kukhala maso (35-40)

    • Mtumiki woyangʼanira nyumba wokhulupirika komanso wosakhulupirika (41-48)

    • Sanabweretse mtendere, koma kudzagawanitsa (49-53)

    • Kufunika kozindikira tanthauzo la zimene zikuchitika (54-56)

    • Kuthetsa mikangano (57-59)

  • 13

    • Lapani apo ayi mudzawonongedwa (1-5)

    • Fanizo la mtengo wa mkuyu wosabereka (6-9)

    • Mzimayi wopindika msana anachiritsidwa tsiku la Sabata (10-17)

    • Fanizo la kanjere ka mpiru komanso la zofufumitsa (18-21)

    • Pakufunika khama kuti tilowe pakhomo lalingʼono (22-30)

    • Herode ananenedwa kuti “nkhandwe” (31-33)

    • Yesu analirira Yerusalemu (34, 35)

  • 14

    • Munthu amene anali ndi manja komanso miyendo yotupa anachiritsidwa tsiku la Sabata (1-6)

    • Mukakhala mlendo muzidzichepetsa (7-11)

    • Muziitana anthu amene sangathe kukubwezerani (12-14)

    • Fanizo la anthu amene anakana kupita kuphwando (15-24)

    • Zimene zimafunika kuti munthu akhale wophunzira (25-33)

    • Mchere umene watha mphamvu (34, 35)

  • 15

    • Fanizo la nkhosa yotayika (1-7)

    • Fanizo la khobidi lotayika (8-10)

    • Fanizo la mwana wolowerera (11-32)

  • 16

    • Fanizo la mtumiki woyangʼanira nyumba wosalungama (1-13)

      • ‘Munthu wokhulupirika pa chinthu chachingʼono amakhalanso wokhulupirika pa chinthu chachikulu’ (10)

    • Chilamulo komanso Ufumu wa Mulungu (14-18)

    • Fanizo la munthu wolemera ndi Lazaro (19-31)

  • 17

    • Kupunthwa, kukhululuka ndi chikhulupiriro (1-6)

    • Akapolo opanda pake (7-10)

    • Anthu 10 akhate anachiritsidwa (11-19)

    • Kubwera kwa Ufumu wa Mulungu (20-37)

      • Ufumu wa Mulungu uli “pakati panu” (21)

      • “Kumbukirani mkazi wa Loti” (32)

  • 18

    • Fanizo la mkazi wamasiye amene anachita khama kupempha (1-8)

    • Mfarisi komanso wokhometsa msonkho (9-14)

    • Yesu ndi ana (15-17)

    • Funso la wolamulira wolemera (18-30)

    • Yesu ananeneratu za imfa yake kachitatu (31-34)

    • Wopemphapempha amene anali wosaona anayamba kuona (35-43)

  • 19

    • Yesu anakacheza kwa Zakeyu (1-10)

    • Fanizo la ndalama zokwana ma mina 10 (11-27)

    • Yesu analowa mumzinda mwaulemerero (28-40)

    • Yesu analirira Yerusalemu (41-44)

    • Yesu anayeretsa kachisi (45-48)

  • 20

    • Anthu anakayikira ulamuliro wa Yesu (1-8)

    • Fanizo la alimi opha anthu (9-19)

    • Mulungu komanso Kaisara (20-26)

    • Funso lokhudza kuuka kwa akufa (27-40)

    • Kodi Khristu ndi mwana wa Davide? (41-44)

    • Anachenjeza anthu kuti asamale ndi alembi (45-47)

  • 21

    • Timakobidi tiwiri ta mkazi wamasiye (1-4)

    • CHIZINDIKIRO CHA ZINTHU ZAMʼTSOGOLO (5-36)

      • Nkhondo, zivomerezi zamphamvu, miliri, kusowa kwa chakudya (10, 11)

      • Yerusalemu adzazunguliridwa ndi magulu ankhondo (20)

      • Nthawi yoikidwiratu ya anthu amitundu ina (24)

      • Kubwera kwa Mwana wa munthu (27)

      • Fanizo la mtengo wa mkuyu (29-33)

      • Khalani maso (34-36)

    • Yesu anaphunzitsa mʼkachisi (37, 38)

  • 22

    • Ansembe anakonza chiwembu kuti aphe Yesu (1-6)

    • Kukonzekera Pasika womaliza (7-13)

    • Kuyambitsa mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye (14-20)

    • “Wondipereka ndili naye limodzi patebulo pompano” (21-23)

    • Anakangana kwambiri za amene anali wamkulu (24-27)

    • Pangano la Yesu la ufumu (28-30)

    • Ananeneratu kuti Petulo adzamukana (31-34)

    • Kufunika kokhala okonzeka; malupanga awiri (35-38)

    • Pemphero la Yesu paphiri la Maolivi (39-46)

    • Yesu anagwidwa (47-53)

    • Petulo anakana Yesu (54-62)

    • Yesu anachitiridwa zachipongwe (63-65)

    • Anamupititsa ku Khoti Lalikulu la Ayuda (66-71)

  • 23

    • Yesu anaonekera pamaso pa Pilato ndi Herode (1-25)

    • Yesu anapachikidwa pamtengo limodzi ndi zigawenga ziwiri (26-43)

      • “Iwe udzakhala ndi ine mʼParadaiso” (43)

    • Imfa ya Yesu (44-49)

    • Kuikidwa mʼmanda kwa Yesu (50-56)

  • 24

    • Yesu anaukitsidwa (1-12)

    • Pamsewu wopita ku Emau (13-35)

    • Yesu anaonekera kwa ophunzira (36-49)

    • Yesu anakwera kumwamba (50-53)