Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la Levitiko

Machaputala

Mitu

  • 1

    • Nsembe yopsereza (1-17)

  • 2

    • Nsembe yambewu (1-16)

  • 3

    • Nsembe yamgwirizano (1-17)

      • Musamadye mafuta kapena magazi (17)

  • 4

    • Nsembe yamachimo (1-35)

  • 5

    • Machimo osiyanasiyana komanso nsembe zake (1-6)

      • Kuulula machimo a anthu ena (1)

    • Nsembe zimene anthu osauka ankapereka (7-13)

    • Nsembe yakupalamula imene munthu amapereka chifukwa chakuti wachimwa mosadziwa (14-19)

  • 6

    • Zinanso zokhudza nsembe yakupalamula (1-7)

    • Malangizo okhudza nsembe (8-30)

      • Nsembe yopsereza (8-13)

      • Nsembe yambewu (14-23)

      • Nsembe yamachimo (24-30)

  • 7

    • Malangizo okhudza nsembe (1-21)

      • Nsembe yakupalamula (1-10)

      • Nsembe yamgwirizano (11-21)

    • Lamulo loletsa kudya mafuta komanso magazi (22-27)

    • Gawo la ansembe (28-36)

    • Mfundo zomaliza zokhudza nsembe (37, 38)

  • 8

    • Kuikidwa unsembe kwa anthu a mʼbanja la Aroni (1-36)

  • 9

    • Aroni anapereka nsembe (1-24)

  • 10

    • Moto wochokera kwa Yehova unapha Nadabu ndi Abihu (1-7)

    • Malamulo opita kwa ansembe okhudza kumwa ndi kudya (8-20)

  • 11

    • Nyama zosadetsedwa ndi zodetsedwa (1-47)

  • 12

    • Kudziyeretsa pambuyo pobereka mwana (1-8)

  • 13

    • Malamulo okhudza khate (1-46)

    • Khate lapachovala (47-59)

  • 14

    • Kudziyeretsa ku khate (1-32)

    • Kuyeretsa nyumba zimene munali nthenda (33-57)

  • 15

    • Kudetsedwa chifukwa cha kukha kumaliseche (1-33)

  • 16

    • Tsiku la Mwambo Wophimba Machimo (1-34)

  • 17

    • Chihema, malo operekera nsembe (1-9)

    • Analetsa kudya magazi (10-14)

    • Malamulo okhudza nyama zopezeka zitafa (15, 16)

  • 18

    • Kugonana kosaloleka (1-30)

      • Musatsanzire Akanani (3)

      • Kugonana ndi achibale (6-18)

      • Nthawi imene mkazi akusamba (19)

      • Kugonana amuna kapena akazi okhaokha (22)

      • Kugonana ndi nyama (23)

      • ‘Mukhale oyera, mukapanda kutero dziko lidzakulavulani’ (24-30)

  • 19

    • Malamulo osiyanasiyana okhudza kukhala oyera (1-37)

      • Kakololedwe koyenera (9, 10)

      • Kuchita zinthu moganizira anthu avuto losaona ndi losamva (14)

      • Miseche (16)

      • Musamasunge chakukhosi (18)

      • Analetsa kuchita zamatsenga ndi zamizimu (26, 31)

      • Analetsa kudzichekacheka (28)

      • Kulemekeza achikulire (32)

      • Zoyenera kuchita ndi alendo (33, 34)

  • 20

    • Kulambira Moleki; zamizimu (1-6)

    • Mukhale oyera ndipo muzilemekeza makolo (7-9)

    • Opalamula milandu yokhudza kugonana ayenera kuphedwa (10-21)

    • Mukhale oyera kuti mupitirize kukhala mʼdziko (22-26)

    • Anthu ochita zamizimu aziphedwa (27)

  • 21

    • Ansembe azikhala oyera komanso osadetsedwa (1-9)

    • Mkulu wa ansembe asamadzidetse (10-15)

    • Ansembe asamakhale ndi chilema (16-24)

  • 22

    • Kuyeretsedwa kwa ansembe komanso kudya zinthu zopatulika (1-16)

    • Nyama zopanda chilema zokha ndi zimene ziyenera kuperekedwa nsembe (17-33)

  • 23

    • Masiku opatulika komanso zikondwerero (1-44)

      • Sabata (3)

      • Pasika (4, 5)

      • Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa (6-8)

      • Nsembe za zipatso zoyambirira (9-14)

      • Zikondwerero za Masabata (15-21)

      • Kakololedwe koyenera (22)

      • Mwambo Woliza Lipenga (23-25)

      • Tsiku la Mwambo Wophimba Machimo (26-32)

      • Chikondwerero cha Misasa (33-43)

  • 24

    • Mafuta a nyale zamuchihema (1-4)

    • Mitanda ya mkate wachionetsero (5-9)

    • Munthu wonyoza dzina la Mulungu aziponyedwa miyala (10-23)

  • 25

    • Chaka cha Sabata (1-7)

    • Chaka cha Ufulu (8-22)

    • Kubweza katundu kwa mwiniwake (23-34)

    • Zoyenera kuchita ndi anthu osauka (35-38)

    • Malamulo okhudza ukapolo (39-55)

  • 26

    • Muzipewa kulambira mafano (1, 2)

    • Madalitso obwera chifukwa cha kumvera (3-13)

    • Chilango cha munthu wosamvera (14-46)

  • 27

    • Kuwombola zinthu zimene zinaperekedwa mochita kulonjeza (1-27)

    • Zinthu zoyenera kuwonongedwa zoperekedwa kwa Yehova (28, 29)

    • Kuwombola chakhumi (30-34)