Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la Hagai

Machaputala

1 2

Mitu

  • 1

    • Anadzudzula anthu chifukwa chosamanganso kachisi (1-11)

      • ‘Kodi ino ndi nthawi yoti inu muzikhala mʼnyumba zokongoletsedwa ndi matabwa?’ (4)

      • “Ganizirani mofatsa zimene mukuchita” (5)

      • Kudzala zambiri nʼkukolola zochepa (6)

    • Anthu anamvera mawu a Yehova (12-15)

  • 2

    • Kachisi wachiwiri adzadzaza ndi ulemerero (1-9)

      • Kugwedeza mitundu yonse ya anthu (7)

      • Zinthu zamtengo wapatali zochokera ku mitundu ya anthu zidzabwera (7)

    • Madalitso obwera chifukwa chomanganso kachisi (10-19)

      • Chopatulika sichingachititse kuti chodetsedwa chikhale chopatulika (10-14)

    • Uthenga wopita kwa Zerubabele (20-23)

      • “Ndidzachititsa kuti ukhale ngati mphete yodindira” (23)