Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la Habakuku

Machaputala

1 2 3

Mitu

  • 1

    • Mneneri anapempha thandizo (1-4)

      • ‘Inu Yehova, mpaka liti?’ (2)

      • “Nʼchifukwa chiyani mukulekerera kuponderezana?” (3)

    • Mulungu anagwiritsa ntchito Akasidi popereka chiweruzo (5-11)

    • Mneneri anachonderera Yehova (12-17)

      • ‘Inu Mulungu wanga, simufa’ (12)

      • ‘Ndinu woyera moti simungaonerere zinthu zoipa’ (13)

  • 2

    • ‘Ndidzakhala tcheru kuti ndione zimene adzanene’ (1)

    • Zimene Yehova anayankha mneneri (2-​20)

      • ‘Uziyembekezerabe masomphenyawo’ (3)

      • Wolungama adzakhala ndi moyo chifukwa cha kukhulupirika (4)

      • Masoka 5 a Akasidi (6-20)

        • Anthu odziwa Yehova adzadzaza dziko lapansi (14)

  • 3

    • Mneneri anapemphera kwa Yehova kuti achitepo kanthu (1-19)

      • Mulungu adzapulumutsa anthu ake odzozedwa (13)

      • Kusangalala chifukwa cha Yehova ngakhale pali mavuto (17, 18)