Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la Ezara

Machaputala

1 2 3 4 5 6 7 8 9 10

Mitu

  • 1

    • Mfumu Koresi inalamula kuti kachisi amangidwenso (1-4)

    • Kukonzekera kuchoka ku ukapolo ku Babulo (5-11)

  • 2

    • Anthu amene anabwerera kuchokera ku ukapolo (1-67)

      • Atumiki a pakachisi (43-54)

      • Ana a atumiki a Solomo (55-57)

    • Zopereka zaufulu pakachisi (68-70)

  • 3

    • Anamanganso guwa nʼkuperekapo nsembe (1-6)

    • Ntchito yomanganso kachisi inayambika (7-9)

    • Anamanga maziko a kachisi (10-13)

  • 4

    • Anthu ankatsutsa ntchito yomanganso kachisi (1-6)

    • Adani analemba kalata kwa Mfumu Aritasasita (7-16)

    • Zomwe Aritasasita anayankha (17-22)

    • Ntchito yomanga kachisi inaimitsidwa (23, 24)

  • 5

    • Ayuda anayambiranso kumanga kachisi (1-5)

    • Tatenai analembera kalata Mfumu Dariyo (6-17)

  • 6

    • Dariyo anafufuza nʼkupereka lamulo (1-12)

    • Kachisi anamalizidwa nʼkutseguliridwa (13-18)

    • Anachita Pasika (19-22)

  • 7

    • Ezara anapita ku Yerusalemu (1-10)

    • Aritasasita analembera Ezara kalata (11-26)

    • Ezara anatamanda Yehova (27, 28)

  • 8

    • Anthu amene anabwerera ndi Ezara (1-14)

    • Kukonzekera ulendo (15-30)

    • Kunyamuka ku Babulo nʼkufika ku Yerusalemu (31-36)

  • 9

    • Aisiraeli anakwatira akazi a mitundu ina (1-4)

    • Pemphero la Ezara lovomereza machimo (5-15)

  • 10

    • Pangano loti achotse akazi a mitundu ina (1-14)

    • Akazi a mitundu ina anatumizidwa kwawo (15-44)