Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la Amosi

Machaputala

1 2 3 4 5 6 7 8 9

Mitu

  • 1

    • Amosi analandira uthenga wochokera kwa Yehova (1, 2)

    • Ziweruzo chifukwa chogalukira mobwerezabwereza (3-15)

  • 2

    • Ziweruzo chifukwa chogalukira mobwerezabwereza (1-16)

  • 3

    • Kulengeza uthenga wachiweruzo wa Mulungu (1-8)

      • Mulungu anaulula chinsinsi chake (7)

    • Uthenga wotsutsana ndi Samariya (9-15)

  • 4

    • Uthenga wotsutsana ndi ngʼombe za ku Basana (1-3)

    • Yehova ananyoza kulambira kwabodza kwa Aisiraeli (4, 5)

    • Aisiraeli anakana kubwerera kwa Mulungu (6-13)

      • “Konzekera kukumana ndi Mulungu wako” (12)

      • ‘Mulungu amafotokozera munthu zimene akuganiza’ (13)

  • 5

    • Isiraeli anali ngati namwali wakugwa (1-3)

    • Funafunani Mulungu kuti mukhale ndi moyo (4-17)

      • Muzidana ndi zoipa nʼkumakonda zabwino (15)

    • Tsiku la Yehova ndi tsiku lamdima (18-27)

      • Nsembe za Aisiraeli zinakanidwa (22)

  • 6

    • Tsoka kwa anthu okhala mosatekeseka (1-14)

      • Mabedi aminyanga ya njovu; makapu a vinyo (4, 6)

  • 7

    • Masomphenya osonyeza kuti mapeto a Aisiraeli ali pafupi (1-9)

      • Dzombe (1-3), moto (4-6), chingwe choyezera (7-9)

    • Amosi anauzidwa kuti asiye kunenera (10-17)

  • 8

    • Masomphenya a dengu la zipatso zamʼchilimwe (1-3)

    • Anthu opondereza anzawo anadzudzulidwa (4-14)

      • Njala yauzimu (11)

  • 9

    • Nʼzosatheka kuthawa chiweruzo cha Mulungu (1-10)

    • Nyumba ya Davide inadzutsidwanso (11-15)