Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kalata Yopita kwa Aheberi

Machaputala

1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 11 12 13

Mitu

  • 1

    • Mulungu akulankhula kudzera mwa Mwana wake (1-4)

    • Mwana ndi wamkulu kuposa angelo (5-14)

  • 2

    • Tiziganizira mozama kuposa nthawi zonse (1-4)

    • Zonse zinaikidwa pansi pa mapazi a Yesu (5-9)

    • Yesu ndiponso abale ake (10-18)

      • Mtumiki Wamkulu wa chipulumutso (10)

      • Mkulu wa ansembe wachifundo (17)

  • 3

    • Yesu ndi wamkulu kuposa Mose (1-6)

      • Zinthu zonse zinapangidwa ndi Mulungu (4)

    • Chenjezo lakuti tisakhale opanda chikhulupiriro (7-19)

      • “Lero mukamva mawu a Mulungu” (7, 15)

  • 4

    • Kuopsa kosalowa mumpumulo wa Mulungu (1-10)

    • Anawalimbikitsa kuti alowe mumpumulo wa Mulungu (11-13)

      • Mawu a Mulungu ndi amoyo (12)

    • Yesu, mkulu wa ansembe wapamwamba (14-16)

  • 5

    • Yesu ndi wapamwamba kuposa akulu ansembe onse (1-10)

      • Mofanana ndi unsembe wa Melekizedeki (6, 10)

      • Anaphunzira kumvera chifukwa cha mavuto (8)

      • Ali ndi udindo wopulumutsa kwamuyaya (9)

    • Anawachenjeza zoti asakhale ngati ana (11-14)

  • 6

    • Yesetsani kuti mukhale aakulu mwauzimu (1-3)

    • Anthu amene agwa akupachika kachiwiri Mwana wa Mulungu (4-8)

    • Chiyembekezo chanu chikhale chotsimikizika (9-12)

    • Malonjezo a Mulungu ndi odalirika (13-20)

      • Lonjezo ndiponso lumbiro la Mulungu sizisintha (17, 18)

  • 7

    • Melekizedeki anali mfumu komanso wansembe wapadera (1-10)

    • Khristu ndi wansembe wapamwamba (11-28)

      • Khristu akhoza kupulumutsa anthu (25)

  • 8

    • Chihema chinkachitira chithunzi zinthu zakumwamba (1-6)

    • Kusiyana pakati pa pangano lakale ndi latsopano (7-13)

  • 9

    • Utumiki wopatulika mʼmalo oyera apadziko lapansi (1-10)

    • Khristu anapita kumwamba ndi magazi ake (11-28)

      • Mkhalapakati wa pangano latsopano (15)

  • 10

    • Nsembe za nyama zinali zosakwanira (1-4)

      • Chilamulo chinkachitira chithunzi zinthu zabwino (1)

    • Nsembe ya Khristu ndi yothandiza mpaka kalekale (5-18)

    • Njira yatsopano komanso yamoyo (19-25)

      • Tisaleke kusonkhana pamodzi (24, 25)

    • Anawachenjeza zokhudza kuchimwa mwadala (26-31)

    • Tizikhala olimba mtima komanso achikhulupiriro kuti tipirire (32-39)

  • 11

    • Tanthauzo la chikhulupiriro (1, 2)

    • Zitsanzo za anthu achikhulupiriro (3-40)

      • Popanda chikhulupiriro sitingasangalatse Mulungu (6)

  • 12

    • Yesu, Wokwaniritsa chikhulupiriro chathu (1-3)

      • Gulu lalikulu la mboni (1)

    • Osapeputsa chilango cha Yehova (4-11)

    • Muziwongola njira zimene mapazi anu akuyendamo (12-17)

    • Kufika ku Yerusalemu wakumwamba (18-29)

  • 13

    • Malangizo omaliza ndiponso kupereka moni (1-25)

      • Musaiwale kuchereza alendo (2)

      • Ukwati ukhale wolemekeza (4)

      • Muzimvera amene akukutsogolerani (7, 17)

      • Kupereka nsembe zotamanda Mulungu (15, 16)