Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kalata Yopita kwa Aefeso

Machaputala

1 2 3 4 5 6

Mitu

  • 1

    • Moni (1, 2)

    • Madalitso auzimu (3-7)

    • Kusonkhanitsa zinthu zonse kwa Akhristu (8-14)

      • Kukhazikitsa “dongosolo” pa nthawi imene anaikiratu (10)

      • Anaikidwa chidindo ndi mzimu woyera ngati “chikole chotsimikizira” (13, 14)

    • Paulo anathokoza Mulungu chifukwa cha chikhulupiriro cha Aefeso ndipo anawapempherera (15-23)

  • 2

    • Anapangitsa kuti akhale amoyo mogwirizana ndi Khristu (1-10)

    • Anagwetsa khoma lomwe linkawalekanitsa (11-22)

  • 3

    • Chinsinsi chopatulika chinaphatikizapo anthu a mitundu ina (1-13)

      • Anthu a mitundu ina adzalamulira limodzi ndi Khristu (6)

      • Cholinga chamuyaya cha Mulungu (11)

    • Anapempherera Aefeso kuti akhale ozindikira (14-21)

  • 4

    • Ogwirizana mʼthupi la Khristu (1-16)

      • Mphatso za amuna (8)

    • Umunthu wakale komanso watsopano (17-32)

  • 5

    • Malankhulidwe komanso khalidwe loyera (1-5)

    • Muziyenda ngati ana a kuwala (6-14)

    • Mudzazidwe ndi mzimu (15-20)

      • Muzigwiritsa ntchito bwino nthawi yanu (16)

    • Malangizo opita kwa amuna ndi akazi apabanja (21-33)

  • 6

    • Malangizo opita kwa makolo ndi ana (1-4)

    • Malangizo opita kwa akapolo ndi ambuye (5-9)

    • Zida zonse zankhondo zochokera kwa Mulungu (10-20)

    • Moni womaliza (21-24)