Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kalata Yachiwiri Yopita kwa Timoteyo

Machaputala

1 2 3 4

Mitu

  • 1

    • Moni (1, 2)

    • Paulo anayamikira Mulungu chifukwa cha chikhulupiriro cha Timoteyo (3-5)

    • Kukolezera moto mphatso yochokera kwa Mulungu (6-11)

    • Gwiritsitsabe mawu olondola (12-14)

    • Adani ndi anzake a Paulo (15-18)

  • 2

    • Kuphunzitsa oyenerera kukhala aphunzitsi (1-7)

    • Kuvutika chifukwa cha uthenga wabwino (8-13)

    • Kufotokoza bwino mawu a choonadi (14-19)

    • Kuthawa zilakolako za unyamata (20-22)

    • Zoyenera kuchita ndi otsutsa (23-26)

  • 3

    • Masiku otsiriza adzakhala nthawi yovuta (1-7)

    • Kutsatira chitsanzo cha Paulo (8-13)

    • “Pitiriza kutsatira zimene unaphunzira” (14-17)

      • Malemba onse anauziridwa ndi Mulungu (16)

  • 4

    • “Uzikwaniritsa mbali zonse za utumiki wako” (1-5)

      • Lalikira mawu modzipereka (2)

    • “Ndamenya nkhondo yabwino” (6-8)

    • Zina zomwe Paulo ananena (9-18)

    • Kupereka moni (19-22)