Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la 2 Samueli

Machaputala

Mitu

  • 1

    • Davide anamva za imfa ya Sauli (1-16)

    • Davide anaimba nyimbo yolira Sauli ndi Yonatani (17-27)

  • 2

    • Davide anakhala mfumu ya Yuda (1-7)

    • Isi-boseti anakhala mfumu ya Isiraeli (8-11)

    • Nkhondo ya pakati pa anthu a Davide ndi anthu a Sauli (12-32)

  • 3

    • Davide anakhala wamphamvu (1)

    • Ana a Davide (2-5)

    • Abineri anakhala mbali ya Davide (6-21)

    • Yowabu anapha Abineri (22-30)

    • Davide analira maliro a Abineri (31-39)

  • 4

    • Isi-boseti anaphedwa (1-8)

    • Davide anapha anthu amene anapha Isi-boseti (9-12)

  • 5

    • Davide anakhala mfumu ya Aisiraeli onse (1-5)

    • Yerusalemu analandidwa (6-16)

      • Ziyoni, Mzinda wa Davide (7)

    • Davide anagonjetsa Afilisiti (17-25)

  • 6

    • Likasa analibweretsa ku Yerusalemu (1-23)

      • Uza anagwira Likasa nʼkuphedwa (6-8)

      • Mikala ananyoza Davide (16, 20-23)

  • 7

    • Davide anamuletsa kumanga kachisi (1-7)

    • Pangano la ufumu ndi Davide (8-17)

    • Pemphero la Davide loyamikira (18-29)

  • 8

    • Davide anapambana pa nkhondo (1-14)

    • Ulamuliro wa Davide (15-18)

  • 9

    • Davide anasonyeza Mefiboseti chikondi chokhulupirika (1-13)

  • 10

    • Anagonjetsa Aamoni ndi Asiriya (1-19)

  • 11

    • Davide anachita chigololo ndi Bati-seba (1-13)

    • Davide anakonza zoti Uriya aphedwe (14-25)

    • Davide anakwatira Bati-seba (26, 27)

  • 12

    • Natani anadzudzula Davide (1-15a)

    • Mwana wa Bati-seba anamwalira (15b-23)

    • Bati-seba anabereka Solomo (24, 25)

    • Mzinda wa Aamoni wa Raba unalandidwa (26-31)

  • 13

    • Aminoni anagwiririra Tamara (1-22)

    • Abisalomu anapha Aminoni (23-33)

    • Abisalomu anathawira ku Gesuri  (34-39)

  • 14

    • Yowabu anatuma mzimayi wa ku Tekowa (1-17)

    • Davide anatulukira mapulani a Yowabu (18-20)

    • Abisalomu analoledwa kuti abwerere (21-33)

  • 15

    • Chiwembu cha Abisalomu (1-12)

    • Davide anathawa mu Yerusalemu (13-30)

    • Ahitofeli anagwirizana ndi Abisalomu (31)

    • Husai anatumidwa kukasokoneza malangizo a Ahitofeli (32-37)

  • 16

    • Ziba ananamizira Mefiboseti (1-4)

    • Simeyi ananyoza Davide (5-14)

    • Abisalomu anamulandira Husai (15-19)

    • Malangizo a Ahitofeli (20-23)

  • 17

    • Husai anasokoneza malangizo a Ahitofeli (1-14)

    • Davide anachenjezedwa ndipo anathawa Abisalomu (15-29)

      • Barizilai ndi anthu ena anapereka zakudya (27-29)

  • 18

    • Abisalomu anagonjetsedwa ndipo anafa (1-18)

    • Davide anauzidwa za imfa ya Abisalomu (19-33)

  • 19

    • Davide analira Abisalomu (1-4)

    • Yowabu anadzudzula Davide (5-8a)

    • Davide anabwerera ku Yerusalemu (8b-15)

    • Simeyi anapempha kuti amukhululukire (16-23)

    • Mefiboseti anasonyeza kuti anali wosalakwa (24-30)

    • Barizilai analemekezedwa (31-40)

    • Mkangano pakati pa mafuko (41-43)

  • 20

    • Sheba anaukira Davide; Yowabu anapha Amasa (1-13)

    • Anthu anasakasaka Sheba ndipo anadulidwa mutu (14-22)

    • Ulamuliro wa Davide (23-26)

  • 21

    • Agibiyoni anabwezera anthu a mʼbanja la Sauli (1-14)

    • Nkhondo yolimbana ndi Afilisiti (15-22)

  • 22

    • Davide anatamanda Mulungu chifukwa chowapulumutsa (1-51)

      • “Yehova ndi thanthwe langa” (2)

      • Yehova amakhala wokhulupirika kwa okhulupirika (26)

  • 23

    • Mawu omaliza a Davide (1-7)

    • Zimene asilikali amphamvu a Davide anachita (8-39)

  • 24

    • Davide anachimwa powerenga anthu (1-14)

    • Mliri unapha anthu 70,000 (15-17)

    • Davide anamanga guwa (18-25)

      • Sanapereke nsembe popanda kulipira (24)