Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la 2 Mafumu

Machaputala

Mitu

  • 1

    • Eliya analosera za imfa ya Ahaziya (1-18)

  • 2

    • Eliya anatengedwa ndi mphepo yamkuntho (1-18)

      • Elisa anatenga chovala chauneneri cha Eliya (13, 14)

    • Elisa anachititsa kuti madzi a ku Yeriko akhale abwino (19-22)

    • Zimbalangondo zinapha anyamata a ku Beteli (23-25)

  • 3

    • Yehoramu, mfumu ya Isiraeli (1-3)

    • Amowabu anagalukira Isiraeli (4-25)

    • Amowabu anagonjetsedwa (26, 27)

  • 4

    • Elisa anachulukitsa mafuta a mkazi wamasiye (1-7)

    • Mtima wochereza wa mayi wa ku Sunemu (8-16)

    • Mayi anakhala ndi mwana; mwanayo anamwalira (17-31)

    • Elisa anaukitsa mwana (32-37)

    • Elisa anachotsa poizoni mʼchakudya (38-41)

    • Elisa anachulukitsa mikate (42-44)

  • 5

    • Elisa anachiritsa khate la Namani (1-19)

    • Gehazi wadyera anakhala wakhate (20-27)

  • 6

    • Elisa anayandamitsa nkhwangwa (1-7)

    • Elisa ndi Asiriya (8-23)

      • Maso a mtumiki wa Elisa anatsegulidwa (16, 17)

      • Asiriya anachititsidwa khungu lamaganizo (18, 19)

    • Mumzinda wa Samariya munali njala chifukwa choti unazunguliridwa (24-33)

  • 7

    • Elisa analosera za kutha kwa njala (1, 2)

    • Chakudya chinangosiyidwa mumsasa wa Asiriya (3-15)

    • Ulosi wa Elisa unakwaniritsidwa (16-20)

  • 8

    • Mayi wa ku Sunemu anabwezeredwa malo ake (1-6)

    • Elisa, Beni-hadadi ndi Hazaeli (7-15)

    • Yehoramu, mfumu ya Yuda (16-24)

    • Ahaziya, mfumu ya Yuda (25-29)

  • 9

    • Yehu anadzozedwa kukhala mfumu ya Isiraeli (1-13)

    • Yehu anapha Yehoramu ndi Ahaziya (14-29)

    • Yezebeli anaphedwa; agalu anadya thupi lake (30-37)

  • 10

    • Yehu anapha anthu amʼbanja la Ahabu (1-17)

      • Yehonadabu anagwirizana ndi Yehu (15-17)

    • Yehu anapha anthu olambira Baala (18-27)

    • Ulamuliro wa Yehu (28-36)

  • 11

    • Ataliya analanda ufumu (1-3)

    • Yehoasi anavekedwa ufumu mobisa (4-12)

    • Ataliya anaphedwa (13-16)

    • Yehoyada anasintha zinthu (17-21)

  • 12

    • Yehoasi mfumu ya Yuda (1-3)

    • Yehoasi anakonza kachisi (4-16)

    • Asiriya anaukira (17, 18)

    • Yehoasi anaphedwa (19-21)

  • 13

    • Yehoahazi mfumu ya Isiraeli (1-9)

    • Yehoasi mfumu ya Isiraeli (10-13)

    • Elisa anayesa khama la Yehoasi (14-19)

    • Elisa anamwalira; mafupa ake anaukitsa munthu (20, 21)

    • Ulosi womaliza wa Elisa unakwaniritsidwa (22-25)

  • 14

    • Amaziya, mfumu ya Yuda (1-6)

    • Amaziya anamenyana ndi Aedomu ndi Aisiraeli (7-14)

    • Imfa ya Yehoasi wa ku Isiraeli (15, 16)

    • Imfa ya Amaziya (17-22)

    • Yerobowamu Wachiwiri, mfumu ya Isiraeli (23-29)

  • 15

    • Azariya, mfumu ya Yuda (1-7)

    • Mafumu omaliza a Yuda: Zekariya (8-12), Salumu (13-16), Menahemu (17-22), Pekahiya (23-26), Peka (27-31)

    • Yotamu, mfumu ya Yuda (32-38)

  • 16

    • Ahazi, mfumu ya Yuda (1-6)

    • Ahazi anapereka ziphuphu kwa Asuri (7-9)

    • Ahazi anatengera mapulani a guwa la mulungu wonama (10-18)

    • Imfa ya Ahazi (19, 20)

  • 17

    • Hoshiya, mfumu ya Isiraeli (1-4)

    • Kugonjetsedwa kwa Isiraeli (5, 6)

    • Aisiraeli anapita ku ukapolo chifukwa cha mpatuko (7-23)

    • Anthu a mitundu ina anabweretsedwa mʼmizinda ya ku Samariya (24-26)

    • Ku Samariya kunali zipembedzo zosiyanasiyana (27-41)

  • 18

    • Hezekiya, mfumu ya Yuda (1-8)

    • Kugonjetsedwa kwa ufumu wa Isiraeli (9-12)

    • Senakeribu anaukira Yuda (13-18)

    • Rabisake ananyoza Yehova (19-37)

  • 19

    • Hezekiya anapempha thandizo kwa Yehova kudzera mwa Yesaya (1-7)

    • Senakeribu anaopseza Yerusalemu (8-13)

    • Pemphero la Hezekiya (14-19)

    • Yesaya anafotokoza zimene Mulungu anayankha (20-34)

    • Mngelo anapha Asuri 185,000 (35-37)

  • 20

    • Hezekiya anadwala nʼkuchira (1-11)

    • Anthu anatumidwa kuchokera ku Babulo (12-19)

    • Imfa ya Hezekiya (20, 21)

  • 21

    • Manase, mfumu ya Yuda; anapha anthu (1-18)

      • Yerusalemu adzawonongedwa (12-15)

    • Amoni, mfumu ya Yuda (19-26)

  • 22

    • Yosiya, mfumu ya Yuda (1, 2)

    • Malangizo okhudza kukonza kachisi (3-7)

    • Anapeza buku la Chilamulo (8-13)

    • Hulida analosera tsoka (14-20)

  • 23

    • Yosiya anasintha zinthu (1-20)

    • Anachita chikondwerero cha Pasika (21-23)

    • Zinthu zinanso zimene Yosiya anasintha (24-27)

    • Imfa ya Yosiya (28-30)

    • Yehoahazi, mfumu ya Yuda (31-33)

    • Yehoyakimu, mfumu ya Yuda (34-37)

  • 24

    • Kugalukira kwa Yehoyakimu komanso imfa yake (1-7)

    • Yehoyakini, mfumu ya Yuda (8, 9)

    • Ayuda oyamba kupita ku Babulo (10-17)

    • Zedekiya, mfumu ya Yuda; anagalukira (18-20)

  • 25

    • Nebukadinezara anazungulira Yerusalemu (1-7)

    • Yerusalemu ndi kachisi wake anawonongedwa; Ayuda enanso anapita ku Babulo (8-21)

    • Gedaliya anaikidwa kuti azilamulira (22-24)

    • Gedaliya anaphedwa; anthu anathawira ku Iguputo (25, 26)

    • Yehoyakini anamasulidwa ku Babulo (27-30)