Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kalata Yoyamba ya Yohane

Machaputala

1 2 3 4 5

Mitu

  • 1

    • Mawu opatsa moyo (1-4)

    • Muziyenda mʼkuwala (5-7)

    • Tiyenera kuvomereza machimo (8-10)

  • 2

    • Yesu, nsembe yophimba machimo (1, 2)

    • Kusunga malamulo ake (3-11)

      • Lamulo lakale komanso latsopano (7, 8)

    • Chifukwa cholembera kalatayi (12-14)

    • Musamakonde dziko (15-17)

    • Tichenjere ndi wokana Khristu (18-29)

  • 3

    • Ndife ana a Mulungu (1-3)

    • Ana a Mulungu ndiponso ana a Mdyerekezi (4-12)

      • Yesu adzawononga ntchito za Mdyerekezi (8)

    • Muzikondana (13-18)

    • Mulungu ndi wamkulu kuposa mitima yathu (19-24)

  • 4

    • Muzifufuza mawu ouziridwa (1-6)

    • Kudziwa komanso kukonda Mulungu (7-21)

      • “Mulungu ndi chikondi” (8, 16)

      • Munthu wachikondi sachita mantha (18)

  • 5

    • Amene amakhulupirira Yesu amagonjetsa dziko (1-12)

      • Tanthauzo la kukonda Mulungu (3)

    • Tizikhulupirira kuti pemphero ndi lamphamvu (13-17)

    • Tizisamala mʼdziko loipali (18-21)

      • Dziko lonse lili mʼmanja mwa woipayo (19)