Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kalata Yoyamba Yopita kwa Timoteyo

Machaputala

1 2 3 4 5 6

Mitu

  • 1

    • Moni (1, 2)

    • Chenjezo lokhudza aphunzitsi abodza (3-11)

    • Paulo anasonyezedwa kukoma mtima kwakukulu (12-16)

    • Mfumu yamuyaya (17)

    • “Kumenya nkhondo yabwino” (18-20)

  • 2

    • Kupempherera anthu osiyanasiyana (1-7)

      • Mulungu mmodzi, mkhalapakati mmodzi (5)

      • Dipo lokwanira ndendende (6)

    • Malangizo kwa amuna ndi akazi (8-15)

      • Kuvala mwaulemu (9, 10)

  • 3

    • Zoyenera kuti munthu akhale woyangʼanira (1-7)

    • Zoyenera kuti munthu akhale mtumiki wothandiza (8-13)

    • Chinsinsi chopatulika cha kudzipereka kwa Mulungu (14-16)

  • 4

    • Chenjezo lokhudza zomwe ziwanda zimaphunzitsa (1-5)

    • Kukhala mtumiki wabwino wa Khristu (6-10)

      • Kulimbitsa thupi ndiponso kudzipereka kwa Mulungu (8)

    • Uzisamala ndi zimene umaphunzitsa (11-16)

  • 5

    • Zoyenera kuchita ndi achikulire komanso achinyamata (1, 2)

    • Kuthandiza akazi amasiye (3-16)

      • Kusamalira banja (8)

    • Kulemekeza akulu akhama (17-25)

      • ‘Vinyo pangʼono, chifukwa cha vuto la mʼmimba’ (23)

  • 6

    • Akapolo azilemekeza ambuye awo (1, 2)

    • Aphunzitsi onyenga ndiponso kukonda ndalama (3-10)

    • Malangizo kwa munthu wa Mulungu (11-16)

    • Kulemera pa ntchito zabwino (17-19)

    • Sunga zimene unalandira (20, 21)