Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la 1 Samueli

Machaputala

Mitu

  • 1

    • Elikana ndi akazi ake (1-8)

    • Hana anapemphera kuti akhale ndi mwana (9-18)

    • Samueli anabadwa nʼkuperekedwa kwa Yehova (19-28)

  • 2

    • Pemphero la Hana (1-11)

    • Machimo a ana awiri a Eli (12-26)

    • Yehova anaweruza banja la Eli (27-36)

  • 3

    • Samueli anaitanidwa kuti akhale mneneri (1-21)

  • 4

    • Afilisiti analanda Likasa (1-11)

    • Eli ndi ana ake anafa (12-22)

  • 5

    • Likasa linakhala mʼdziko la Afilisiti (1-12)

      • Dagoni anachititsidwa manyazi (1-5)

      • Afilisiti analangidwa (6-12)

  • 6

    • Afilisiti anabweza Likasa kwa Aisiraeli (1-21)

  • 7

    • Likasa ku Kiriyati-yearimu (1)

    • Samueli anati: ‘Muzitumikira Yehova yekha’ (2-6)

    • Aisiraeli anapambana ku Mizipa (7-14)

    • Samueli anayamba kuweruza Aisiraeli (15-17)

  • 8

    • Aisiraeli anati akufuna mfumu (1-9)

    • Samueli anachenjeza anthu (10-18)

    • Yehova anawapatsa mfumu (19-22)

  • 9

    • Samueli anakumana ndi Sauli (1-27)

  • 10

    • Sauli anadzozedwa kuti akhale mfumu (1-16)

    • Sauli anaonetsedwa kwa anthu (17-27)

  • 11

    • Sauli anagonjetsa Aamoni (1-11)

    • Sauli analongedwa ufumu (12-15)

  • 12

    • Mawu omaliza a Samueli (1-25)

      • ‘Musamatsatire milungu yopanda pake’ (21)

      • Yehova sadzasiya anthu ake (22)

  • 13

    • Sauli anasankha asilikali (1-4)

    • Sauli anachita zinthu modzikuza (5-9)

    • Samueli anadzudzula Sauli (10-14)

    • Aisiraeli analibe zida (15-23)

  • 14

    • Zimene Yonatani anachita ku Mikimasi (1-14)

    • Mulungu anagonjetsa adani a Aisiraeli (15-23)

    • Sauli analumbira mopupuluma (24-46)

      • Anthu anadya nyama ndi magazi omwe (32-34)

    • Nkhondo za Sauli; banja lake (47-52)

  • 15

    • Sauli sanamvere ndipo sanaphe Agagi (1-9)

    • Samueli anadzudzula Sauli (10-23)

      • “Kumvera kumaposa nsembe” (22)

    • Sauli anakanidwa kuti asakhalenso mfumu (24-29)

    • Samueli anapha Agagi (30-35)

  • 16

    • Samueli anadzoza Davide kukhala mfumu yotsatira (1-13)

      • “Yehova amaona mumtima” (7)

    • Mzimu wa Mulungu unamuchokera Sauli (14-17)

    • Davide ankaimbira Sauli zeze (18-23)

  • 17

    • Davide anagonjetsa Goliyati (1-58)

      • Goliyati ankanyoza Aisiraeli (8-10)

      • Davide anadzipereka kukamenyana ndi Goliyati (32-37)

      • Davide anamenya nkhondo mʼdzina la Yehova (45-47)

  • 18

    • Ubwenzi wa Davide ndi Yonatani (1-4)

    • Sauli anayamba kuchitira nsanje Davide (5-9)

    • Sauli ankafuna kupha Davide (10-19)

    • Davide anakwatira Mikala mwana wa Sauli (20-30)

  • 19

    • Sauli anapitiriza kudana ndi Davide (1-13)

    • Davide anathawa Sauli (14-24)

  • 20

    • Yonatani anali wokhulupirika kwa Davide (1-42)

  • 21

    • Davide anadya mkate wachionetsero ku Nobu (1-9)

    • Davide ananamizira misala ku Gati (10-15)

  • 22

    • Davide ku Adulamu ndi ku Mizipe (1-5)

    • Sauli anapha ansembe a ku Nobu (6-19)

    • Abiyatara anapulumuka (20-23)

  • 23

    • Davide anapulumutsa mzinda wa Keila (1-12)

    • Sauli ankasakasaka Davide (13-15)

    • Yonatani analimbikitsa Davide (16-18)

    • Sauli anangotsala pangʼono kupeza Davide (19-29)

  • 24

    • Davide sanaphe Sauli (1-22)

      • Davide analemekeza wodzozedwa wa Yehova (6)

  • 25

    • Samueli anamwalira (1)

    • Nabala anakana kuthandiza anyamata a Davide (2-13)

    • Abigayeli anachita zinthu mwanzeru (14-35)

      • ‘Yehova adzakulunga moyo wanu mʼphukusi la moyo’ (29)

    • Yehova anapha Nabala wopanda nzeru (36-38)

    • Abigayeli anakhala mkazi wa Davide (39-44)

  • 26

    • Davide sanaphenso Sauli (1-25)

      • Davide analemekeza wodzozedwa wa Yehova (11)

  • 27

    • Afilisiti anapatsa Davide mzinda wa Zikilaga (1-12)

  • 28

    • Sauli anapita kwa wolankhula ndi mizimu ku Eni-dori (1-25)

  • 29

    • Afilisiti sanakhulupirire Davide (1-11)

  • 30

    • Aamaleki anaukira ndi kutentha mzinda wa Zikalaga (1-6)

      • Davide anapeza mphamvu kwa Mulungu (6)

    • Davide anagonjetsa Aamaleki (7-31)

      • Davide anapulumutsa anthu amene anatengedwa (18, 19)

      • Lamulo la Davide lokhudza zotengedwa kunkhondo (23, 24)

  • 31

    • Imfa ya Sauli ndi ana ake atatu (1-13)