Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la 1 Mbiri

Machaputala

Mitu

  • 1

    • Kuchokera pa Adamu kufika pa Abulahamu (1-27)

    • Mbadwa za Abulahamu (28-37)

    • Aedomu ndi mafumu awo (38-54)

  • 2

    • Ana 12 a Isiraeli (1, 2)

    • Mbadwa za Yuda (3-55)

  • 3

    • Mbadwa za Davide (1-9)

    • Mzere wa mafumu a mʼbanja la Davide (10-24)

  • 4

    • Mbadwa zina za Yuda (1-23)

      • Yabezi ndiponso pemphero lake (9, 10)

    • Mbadwa za Simiyoni (24-43)

  • 5

    • Mbadwa za Rubeni (1-10)

    • Mbadwa za Gadi (11-17)

    • Mbadwa za Hagara zinagonjetsedwa (18-22)

    • Hafu ya fuko la Manase (23-26)

  • 6

    • Mbadwa za Levi (1-30)

    • Oimba pakachisi (31-47)

    • Mbadwa za Aroni (48-53)

    • Kumene Alevi ankakhala (54-81)

  • 7

    • Mbadwa za Isakara (1-5), za Benjamini (6-12), za Nafitali (13), za Manase (14-19), za Efuraimu (20-29), ndi za Aseri (30-40)

  • 8

    • Mbadwa za Benjamini (1-40)

      • Anthu a mʼbanja la Sauli (33-40)

  • 9

    • Mndandanda wa makolo atabwera kuchokera ku ukapolo (1-34)

    • Kubwereza anthu a mʼbanja la Sauli (35-44)

  • 10

    • Imfa ya Sauli ndi ana ake (1-14)

  • 11

    • Aisiraeli onse anadzoza Davide kukhala mfumu (1-3)

    • Davide analanda mzinda wa Ziyoni (4-9)

    • Asilikali amphamvu a Davide (10-47)

  • 12

    • Anthu amene anali kumbali ya ufumu wa Davide (1-40)

  • 13

    • Likasa linatengedwa ku Kiriyati-yearimu (1-14)

  • 14

    • Ufumu wa Davide unakhazikika (1, 2)

    • Banja la Davide (3-7)

    • Afilisiti anagonjetsedwa (8-17)

  • 15

    • Alevi anatenga Likasa kupita nalo ku Yerusalemu (1-29)

      • Mikala ananyoza Davide (29)

  • 16

    • Likasa linaikidwa mutenti (1-6)

    • Nyimbo ya Davide yothokoza (7-36)

      • “Yehova wakhala Mfumu!” (31)

    • Utumiki wa kumene kunali Likasa (37-43)

  • 17

    • Davide anauzidwa kuti sadzamanga kachisi (1-6)

    • Pangano la ufumu ndi Davide (7-15)

    • Pemphero la Davide loyamika (16-27)

  • 18

    • Davide anapambana nkhondo zosiyanasiyana (1-13)

    • Ulamuliro wa Davide (14-17)

  • 19

    • Chipongwe chimene Aamoni anachitira atumiki a Davide (1-5)

    • Aamoni ndi Asiriya anagonjetsedwa (6-19)

  • 20

    • Raba anagonjetsedwa (1-3)

    • Ziphona za Afilisiti zinaphedwa (4-8)

  • 21

    • Davide anawerenga anthu mosavomerezeka (1-6)

    • Chilango chochokera kwa Yehova (7-17)

    • Davide anamanga guwa (18-30)

  • 22

    • Davide anakonzekera zinthu zomangira kachisi (1-5)

    • Davide anapereka malangizo kwa Solomo (6-16)

    • Akalonga analamulidwa kuti athandize Solomo (17-19)

  • 23

    • Davide anapereka ntchito kwa Alevi (1-32)

      • Aroni ndi ana ake anasankhidwa kuti azigwira ntchito yopatulika (13)

  • 24

    • Davide anagawa ansembe mʼmagulu 24 (1-19)

    • Ntchito zina za Alevi (20-31)

  • 25

    • Oimba panyumba ya Mulungu (1-31)

  • 26

    • Magulu a alonda apageti (1-19)

    • Oyangʼanira chuma ndi anthu a maudindo ena (20-32)

  • 27

    • Anthu otumikira mfumu (1-34)

  • 28

    • Zimene Davide ananena zokhudza kumanga kachisi (1-8)

    • Solomo anapatsidwa malangizo komanso mapulani omangira (9-21)

  • 29

    • Zopereka zothandiza pomanga kachisi (1-9)

    • Pemphero la Davide (10-19)

    • Anthu anasangalala; ufumu wa Solomo (20-25)

    • Imfa ya Davide (26-30)