Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kalata Yoyamba Yopita kwa Akorinto

Machaputala

1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 11 12 13 14 15 16

Mitu

  • 1

    • Mawu oyamba (1-3)

    • Paulo anayamikira Mulungu chifukwa cha Akorinto (4-9)

    • Anawalangiza kuti akhale ogwirizana (10-17)

    • Khristu ndi mphamvu komanso nzeru ya Mulungu (18-25)

    • Kudzitama mwa Yehova (26-31)

  • 2

    • Paulo analalikira ku Korinto (1-5)

    • Nzeru za Mulungu ndi zapamwamba (6-10)

    • Kusiyana pakati pa munthu wauzimu ndi munthu wokonda za mʼdziko (11-16)

  • 3

    • Akorinto ankakondabe zinthu za mʼdziko (1-4)

    • Mulungu ndi amene amakulitsa (5-9)

      • Antchito anzake a Mulungu (9)

    • Kumanga ndi zinthu zosagwira moto (10-15)

    • Ndinu kachisi wa Mulungu (16, 17)

    • Nzeru zamʼdziko ndi zopusa kwa Mulungu (18-23)

  • 4

    • Atumiki ayenera kukhala okhulupirika (1-5)

    • Atumiki a Chikhristu ayenera kukhala odzichepetsa (6-13)

      • ‘Musapitirire zolembedwa’ (6)

      • Akhristu akuonetsedwa mʼbwalo lamasewera (9)

    • Paulo ankasamalira ana ake auzimu (14-21)

  • 5

    • Nkhani ya munthu yemwe anachita chiwerewere (1-5)

    • Zofufumitsa zochepa zimafufumitsa mtanda wonse (6-8)

    • Munthu woipa anayenera kuchotsedwa (9-13)

  • 6

    • Akhristu ankatengerana kukhoti (1-8)

    • Anthu amene sadzalowa mu Ufumu (9-11)

    • Lemekezani Mulungu ndi matupi anu (12-20)

      • “Thawani chiwerewere” (18)

  • 7

    • Malangizo a anthu amene sali pabanja ndi amene ali pabanja (1-16)

    • Mukhale mmene munalili pamene munkaitanidwa (17-24)

    • Anthu omwe sali pabanja ndiponso akazi amasiye (25-40)

      • Ubwino wosakhala pabanja (32-35)

      • Kukwatiwa “mwa Ambuye” (39)

  • 8

    • Chakudya choperekedwa kwa mafano (1-13)

      • Kwa ife kuli Mulungu mmodzi (5, 6)

  • 9

    • Chitsanzo cha mtumwi Paulo (1-27)

      • “Usamange ngʼombe pakamwa” (9)

      • ‘Tsoka kwa ine ngati sindilalikira’ (16)

      • Kukhala zinthu zonse kwa anthu onse (19-23)

      • Kudziletsa pa mpikisano wokalandira moyo (24-27)

  • 10

    • Zitsanzo zotichenjeza za Aisiraeli (1-13)

    • Chenjezo pa nkhani yolambira mafano (14-22)

      • Tebulo la Yehova ndiponso tebulo la ziwanda (21)

    • Ufulu ndiponso kuganizira ena (23-33)

      • “Muzichita zinthu zonse kuti zibweretse ulemerero kwa Mulungu” (31)

  • 11

    • “Muzitsanzira ine” (1)

    • Nkhani yokhudza mutu ndiponso kuvala chophimba kumutu (2-16)

    • Mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye (17-34)

  • 12

    • Mphatso za mzimu (1-11)

    • Thupi limodzi, ziwalo zambiri (12-31)

  • 13

    • Chikondi—njira yopambana (1-13)

  • 14

    • Mphatso yonenera ndiponso yolankhula malilime (1-25)

    • Misonkhano izichitika mwadongosolo (26-40)

      • Zimene akazi ayenera kuchita mumpingo (34, 35)

  • 15

    • Kuukitsidwa kwa Khristu (1-11)

    • Kuuka kwa akufa ndi maziko a chikhulupiriro (12-19)

    • Kuuka kwa Khristu kumatitsimikizira kuti akufa adzauka (20-34)

    • Thupi la mnofu ndiponso thupi lauzimu (35-49)

    • Thupi loti silingafe kapena kuwonongeka (50-57)

    • Kuchita zambiri pa ntchito ya Ambuye (58)

  • 16

    • Kutolera zopereka zopita kwa Akhristu a ku Yerusalemu (1-4)

    • Maulendo amene Paulo ankafuna kuyenda (5-9)

    • Ulendo wa Timoteyo ndiponso wa Apolo (10-12)

    • Malangizo ndiponso kupereka moni (13-24)