Pitani ku nkhani yake

Yesu

Kodi Yesu ndi Ndani?

Kodi Yesu Anali Munthu Wabwino Basi?

Chifukwa chimene chinachititsa Yesu wa ku Nazareti kukhala munthu wotchuka kwambiri kuposa anthu onse amene anakhalapo.

Kodi Yesu Ndi Mulungu Wamphamvuyonse?

Kodi Yesu ananena kuti iye ndi wofanana ndi Mulungu?

N’chifukwa Chiyani Baibulo Limati Yesu Ndi Mwana wa Mulungu?

Ngati Mulungu sanabereke Yesu ngati mmene anthu amachitira, n’chifukwa chiyani Baibulo limati Yesu ndi Mwana wa Mulungu?

Kodi Wokana Khristu Amachita Zotani?

Kodi akubwera kapena alipo kale?

Kodi Baibulo Limatanthauza Chiyani Likamanena Kuti “Mawu?”

M’Baibulo, mawu amatanthauza zinthu zingapo

Kodi Mikayeli Mkulu wa Angelo Ndi Ndani?

Amadziwika ndi dzina lina limene mumalidziwa bwino.

Yesu ali Padziko Lapansi

Kodi Yesu Anabadwa Liti?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake anthu amachita Khirisimasi pa December 25.

Kodi Baibulo Limaphunzitsa Zotani Zokhudza Mariya Virigo?

Ena amanena kuti Mariya sanabadwe ndi tchimo lililonse. Kodi Baibulo limati chiyani za nkhaniyi?

Kodi “Anzeru a Kum’mawa” Anali Ndani? Kodi Mulungu Ndi Amene Anawachititsa Kuti Alondole Nyenyezi ya ku Betelehemu?

Miyambo yambiri yomwe imachitika yokhudza Khirisimasi siipezeka n’komwe m’Baibulo.

Kodi Akatswiri a Maphunziro Amakhulupirira Kuti Yesu Anakhalapodi?

Werengani kuti mudziwe ngati ankakhulupirira zoti Yesu anali munthu weniweni kapena ayi.

Kodi Nkhani ya Moyo wa Yesu Imene Ili M’Baibulo Ndi Yolondola?

Dziwani mfundo zokhudza nkhani za m’mabuku a Uthenga Wabwino ndiponso mipukutu yakale kwambiri imene ikudziwika masiku ano.

Kodi Yesu Ankaoneka Bwanji?

Mfundo zina zimene Baibulo limafotokoza zimatithandiza kudziwa mmene Yesu ankaonekera.

Kodi Yesu Anakwatira? Kodi Anali ndi Abale Ake?

Popeza Baibulo silifotokoza mwachindunji zoti Yesu anakwatira kapena ayi, ndiyeno tingadziwe bwanji zoona zake za nkhaniyi?

Kodi Nkhani Zokhudza Moyo wa Yesu Zinalembedwa Liti?

Kodi panapita nthawi yaitali bwanji kuchokera pamene Yesu anafa kufika pamene mabuku a Uthenga Wabwino analembedwa?

Imfa ya Yesu Komanso Kuukitsidwa Kwake

N’chifukwa Chiyani Yesu Anafa?

Anthu ambiri amadziwa mfundo yakuti Yesu anafa ndi cholinga choti tikhale ndi moyo. Koma kodi imfa ya Yesu imatithandiza bwanji kwenikweni?

Kodi Yesu Anafera Pamtanda?

Anthu ambiri amaona kuti mtanda ndi chizindikiro cha Chikhristu. Kodi tiyenera kuugwiritsira ntchito polambira?

Kodi Yesu Atafa Anakulungidwa mu Nsalu ya Maliro Yomwe Inasungidwa ku Turin?

Mfundo zitatu zofunika kwambiri zokhudza nsalu ya maliro zomwe zingatithandize kupeza mayankho.

Kodi Yesu Anaukitsidwa ndi Thupi Lotani?

Baibulo limanena kuti Yesu “anaukitsidwa monga mzimu,” ndiye kodi zinatheka bwanji kuti ophunzira ake amuone?

Udindo wa Yesu Pokwaniritsa Cholinga cha Mulungu

Kodi Yesu Amatipulumutsa Bwanji?

N’chifukwa chiyani Yesu amafunika kuchonderera m’malo mwathu? Kodi kungokhulupirira Yesu n’kokwanira kuti tidzapulumuke?

Kodi Nsembe ya Yesu Imawombola Bwanji “Anthu Ambiri”?

Kodi dipo limawombola bwanji anthu ku uchimo?

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupemphera M’dzina la Yesu?

M’nkhaniyi muona kuti kupemphera m’dzina la Yesu kumasonyeza kuti timalemekeza Mulungu komanso Yesu.

Kodi Kubweranso kwa Yesu Kumatanthauza Chiyani?

Kodi Yesu akamadzabwera, anthu adzamuona?