Pitani ku nkhani yake

Chikhulupiro Komanso Kulambira

Chipembedzo

Kodi Kukhala Munthu Wauzimu N’kutani? Kodi Ndingakhale Munthu Wauzimu Popanda Kukhala M’chipembedzo Chilichonse?

Onani mfundo zitatu zimene zingakuthandizeni kukhala munthu wauzimu komanso maganizo 4 olakwika okhudza anthu auzimu.

Kodi Zipembedzo Zonse N’zofanana Ndipo Zimathandizadi Anthu Kudziwa Mulungu?

Mfundo ziwiri zofotokozedwa m’Baibulo zingatithandize kudziwa yankho la funsoli.

N’chifukwa Chiyani Pali Zipembedzo Zambiri Zimene Zimati N’zachikhristu?

Kodi Yesu amene anayambitsa Chikhristu ankafuna kuti padzakhale zipembedzo zambiri zimene zimati n’zachikhristu?

Kodi Ndingachidziwe Bwanji Chipembedzo Cholondola?

Kodi ineyo ndikuona kuti chimenechi ndi chipembedzodi cholondola?

Kodi Wokana Khristu Amachita Zotani?

Kodi akubwera kapena alipo kale?

Kodi Kukhala Woyera Kumatanthauza Chiyani?

Kodi n’zotheka kuti anthu ochimwafe tikhale oyera?

Pemphero

Kodi Mulungu Angandithandize Ndikapemphera?

Kodi Mulungu zimam’khudza tikamavutika?

Kodi Mulungu Angayankhe Mapemphero Anga?

Kuti Mulungu ayankhe mapemphero anu zimadalira kwambiri pa zimene inuyo mumachita.

Kodi Ndizipemphera Bwanji?—Kodi Ndizigwiritsa Ntchito Pemphero la Ambuye?

Kodi pemphero la Atate Wathu ndi pemphero lokhalo lomwe Mulungu amamva?

Kodi Ndingatchule Zinthu Ziti Popemphera?

M’nkhaniyi muona kuti Mulungu saona kuti nkhani ngati zimenezi ndi zazing’ono.

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupemphera M’dzina la Yesu?

M’nkhaniyi muona kuti kupemphera m’dzina la Yesu kumasonyeza kuti timalemekeza Mulungu komanso Yesu.

Kodi Ndizipemphera kwa Anthu Oyera Mtima?

Dziwani zimene Baibulo limanena pa nkhani yakuti tizipemphera kwa ndani.

N’chifukwa Chiyani Mulungu Samvetsera Mapemphero Ena?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mapemphero amene Mulungu sayankha komanso anthu. Mudziwanso anthu amene Mulungu sawamvetsera akamapemphera.

Kupulumuka

Kodi Chipulumutso N’chiyani?

Kodi tiyenera kuchita chiyani kuti tidzapulumuke? Kodi munthu adzapulumutsidwa ku chiyani?

Kodi Yesu Amatipulumutsa Bwanji?

N’chifukwa chiyani Yesu amafunika kuchonderera m’malo mwathu? Kodi kungokhulupirira Yesu n’kokwanira kuti tidzapulumuke?

N’chifukwa Chiyani Yesu Anafa?

Anthu ambiri amadziwa mfundo yakuti Yesu anafa ndi cholinga choti tikhale ndi moyo. Koma kodi imfa ya Yesu imatithandiza bwanji kwenikweni?

Kodi Nsembe ya Yesu Imawombola Bwanji “Anthu Ambiri”?

Kodi dipo limawombola bwanji anthu ku uchimo?

Kodi Ubatizo Umatanthauza Chiyani?

Baibulo limafotokoza za anthu ambiri amene anabatizidwa m’madzi, zomwe zimasonyeza tanthauzo komanso kufunika kwa ubatizo.

Kodi Kubadwanso Kumatanthauza Chiyani?

Kodi muyenera kubadwanso kuti mukhale Mkhristu?

Kuchimwa Komanso Kukhululuka

Kodi Tchimo Loyambirira Linali Chiyani?

Adamu ndi Hava anapatsira ana awo onse uchimo. Zimenezi n’zofanana ndi zomwe zimachitika ndi makolo omwe apatsira ana awo matenda.

Kodi Tchimo N’chiyani?

Kodi machimo ena amakhala aakulu kuposa ena?

Kodi Kukhululuka Kumatanthauza Chiyani?

M’Baibulo muli mfundo 5 zimene zingatithandize kukhululukira ena.

Kodi Mulungu Angandikhululukire Machimo Anga?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene zingakuthandizeni kuti Mulungu azikukhululukirani zolakwa zanu.

Kodi Baibulo Lingathandize Anthu Amene Amangokhalira Kudziimba Mlandu?

Kudziimba mlandu mopitirira malire kungachititse kuti muzingokhala wokhumudwa nthawi zonse, koma pali mfundo zitatu zomwe zingakuthandizeni kuthana ndi vutoli.

Kodi Pali “Machimo 7 Obweretsa Imfa?”

Kodi zimenezi zinachokera kuti? Nanga kodi tchimo lomwe limabweretsa imfa limasiyana bwanji ndi limene silibweretsa imfa?

Kodi Ndi Tchimo Liti Limene Munthu Sangakhululukidwe?

Kodi mungadziwe bwanji ngati munachita tchimo limene Mulungu sangakukhululukireni?

Kodi Lamulo Lakuti “Diso Kulipira Diso” Limatanthauza Chiyani?

Kodi lamulo lakuti “diso kulipira diso” linkapereka ufulu woti anthu azibwezerana?

Kodi Baibulo Limanena Kuti Kumwa Mowa Ndi Tchimo?

Baibulo limasonyeza kuti mowa ukhoza kuthandiza munthu amene akudwala m’mimba komanso likhoza kuthandiza munthu kuti azisangalala.

Kodi Kusuta Ndi Tchimo?

Popeza kuti m’Baibulo mulibemo nkhani yokhudza kusuta, ndiye zingatheke bwanji kuti liyankhe funso limeneli?

Zimene Zipembedzo Zimaphunzitsa

Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yopereka Chakhumi?

Mungadabwe kudziwa kuti zimene Baibulo limaphunzitsa pa nkhaniyi n’zosiyana kwambiri ndi zimene anthu ena amaganiza.

Kodi Tiyenera Kulambira Mafano?

Kodi Mulungu amasangalala tikamagwiritsa ntchito mafano pomulambira?

Kodi Akhristu Ayenera Kusunga Sabata?

Ngati Akhristu sakuyenera kusunga Sabata n’chifukwa chiyani Baibulo limati ndi lamulo losatha?

Kodi Baibulo Limaphunzitsa Zotani pa Nkhani ya Malilime?

Kodi Akhristu enieni amadziwika ndi malilime?

Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Kusala Kudya?

Kodi anthu otchulidwa m’Baibulo ankasala kudya pa zifukwa ziti? Kodi Akhristu amayenera kusala kudya?

Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Kupatsa?

Kodi Mulungu amasangalala ndi kupatsa kotani?

Kodi Malamulo Khumi a Mulungu Ndi Chiyani?

Kodi malamulowo anaperekedwa kwa ndani? Kodi Akhristu ayenera kuwatsatira?