Pitani ku nkhani yake

Mulungu

Kodi Mulungu ndi Ndani?

Kodi Mulungu Alipodi?

Baibulo limayankha mogwira mtima mafunso 5 ofunika kwambiri.

Kodi Mulungu Ndi Mphamvu Yosaoneka?

Baibulo limanena kuti Mulungu analenga zinthu zonse. Koma kodi iye amatiwerengera?

Kodi Mulungu Amangopezeka Pena Paliponse?

Kodi Baibulo limaphunzitsa kuti Mulungu amangopezeka pena paliponse? N’chiyani chingakuthandizeni kukhulupirira kuti Mulungu ali ndi malo enieni amene amakhala komanso kuti amakudziwani bwino inuyo monga munthu panokha?

Kodi Mulungu Ali ndi Malo Enieni Amene Amakhala?

Kodi Baibulo limati Mulungu amakhala kuti? Kodi Yesu amakhala kumene kuli Mulungu?

Kodi Pali Munthu Amene Anaonapo Mulungu?

Kodi Baibulo limadzitsutsa likamanena kuti “palibe munthu anaonapo Mulungu” komanso likamanena kuti Mose “anaona Mulungu wa Aisiraeli”?

Kodi Baibulo Limaphunzitsa Kuti Pali Mulungu Atate, Mulungu Mwana ndi Mulungu Mzimu mwa Mulungu M’modzi?

Zipembedzo zambiri zimaphunzitsa kuti pali Mulungu Atate, Mulungu Mwana ndi Mulungu Mzimu mwa Mulungu M’modzi. Kodi chiphunzitso chimenechi n’cha m’Baibulo?

Kodi Mariya Ndi Amayi a Mulungu?

Malemba komanso mbiri yonena za mmene Chikhristu chinayambira zimatithandiza kudziwa zoona zokhudza chiphunzitso chimenechi.

Kodi Mulungu Amasintha Maganizo Ake?

Kodi Baibulo limadzitsutsa likamanena kuti Mulungu anati ‘Ine sindisintha’ komanso kuti, “Ndidzasintha maganizo anga?

Kodi Mzimu Woyera N’chiyani?

Pali zifukwa zomveka zimene Baibulo limatchulira mzimu woyera kuti ndi “manja” a Mulungu.

God’s Name

Kodi Mulungu Ali Ndi Dzina?

M’Mabaibulo ambiri muli dzina lenileni la Mulungu. N’chifukwa chiyani muyenera kugwiritsa ntchito dzinali?

Kodi Dzina la Mulungu Ndi Yesu?

Yesu sananenepo kuti iye ndi Mulungu Wamphamvuyonse. N’chifukwa chiyani sanatero?

Kodi Yehova Ndi Ndani?

Kodi iye ndi Mulungu wa mtundu umodzi wa anthu ngati Aisiraeli?

Kodi Mulungu Ali ndi Mayina Angati?

Anthu ena angaganize kuti mayina a Mulungu ndi ‘Allah’ kapena ‘El Shaddai,’ komanso ‘Jehova-Yire’ kapena ‘Alefa ndi Omega.’ Kodi pali vuto ngati titamagwiritsa ntchito dzina lililonse potchula Mulungu?

Kodi “Alefa ndi Omega ndi Ndani”?

N’chifukwa chiyani dzina limeneli ndi loyenera?

Chifuniro cha Mulungu

Kodi Mulungu Amafuna Kuti Ndizichita Chiyani?

Kodi mukufunika kuona masomphenya kapena chizindikiro chinachake kuti mudziwe zimene Mulungu akufuna kuti muzichita? Werengani nkhaniyi kuti mudziwe yankho la m’Baibulo.

Kodi Baibulo Limati Mungasankhe Nokha Zochita Kapena Mulungu Analemberatu Tsogolo Lanu?

Anthu ambiri amakhulupirira kuti Mulungu analemberatu tsogolo lathu. Kodi zimene timasankha zimakhudza tsogolo lathu?

Kodi N’chiyani Chingakuthandizeni Kudziwa Bwino Mulungu?

Zinthu 7 zimene zingathandize kuti mukhale pa ubwenzi wabwino ndi Mulungu.

Kodi Mulungu Ndi Amene Amachititsa Kuti Tizivutika?

N’chifukwa chiyani munthu aliyense amavutika, ngakhale amene Mulungu amamukonda?