Nkhani Zinanso

Mpambo umenewu ni wa nkhani zosiyana-siyana zimenenso zili pa tsamba loyamba la jw.org. Lolani kuti nkhani zimenezi na mavidiyo akuthandizeni kulimbitsa cikhulupililo canu pogwilitsa nchito nzelu za m’Baibo.

KHALANI MASO!

Kuwonjezeka kwa Kusamvela Malamulo Padziko Lonse—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Dziwani cimene cikupangitsa kusamvela malamulo kumene tikuona padziko lonse.

KHALANI MASO!

Makhalidwe Aloŵa Pansi—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Makhalidwe aloŵa pansi kwambili kuposa n’kale lonse. Baibo imafotokoza cifukwa cake ndipo imapeleka malangizo odalilika amene angathandize kuti tizikhala aulemu m’zokamba na zocita zathu.

KHALANI MASO!

Kodi Nkhondo Zidzatha Liti?—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Posacedwa, nkhondo zonse zidzatha. Baibo imafotokoza mmene nkhondo zidzathela.

KAMPENI YOITANILA ANTHU KU CIKUMBUTSO

Yesu Adzacotsapo Anthu Osamvela Malamulo

Kodi tingaonetse bwanji kuti timayamikila zimene Yesu anaticitila komanso zimene adzaticitila m’tsogolo?

KAMPENI YOITANILA ANTHU KU CIKUMBUTSO

Yesu Adzathetsa Umphawi

Kodi tingaonetse bwanji kuti timayamikila zimene Yesu anaticitila komanso zimene adzaticitila mtsogolo?

KAMPENI YOITANILA ANTHU KU CIKUMBUTSO

Yesu Adzathetsa Nkhondo

Ndalama Matililiyoni Zawonongedwa pa Nkhondo—Koma Kodi ni Ndalama Zokha Zawonongeka?

Dziŵani cifukwa cake posacedwapa cuma ca dzikoli sicidzagwilitsidwanso nchito pa nkhondo. Komanso onani mmene mavuto obwela cifukwa ca nkhondo adzathela.

Baibo Ingakuthandizeni Kupeza Anzanu Abwino Kuti Muthetse Vuto Losoŵa Woceza Naye

Onani mfundo ziŵili za m’Baibo zimene zingakuthandizeni kuthetsa vuto la kusoŵa woceza naye.

KHALANIBE MASO!

Anthu Ambili Aleka Kukhulupilila Atsogoleli a Ndale—Kodi Baibo Imatipo Ciyani?

Baibo imatilimbikitsa kuti tisamangokhulupilila aliyense, ndipo imatiuza munthu yekhayo amene tiyenela kum’khulupilila kuti tikhale na tsogolo labwino.

KHALANI MASO!

Kodi Nkhondo Ina ya Padziko Lonse Yatsala Pang’ono Kucitika?—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Baibo inakambilatu za kuculuka kwa nkhondo zimene tikuona masiku ano, komanso mmene nkhondo zonsezi zidzathela.

Zimene Baibo Ikambapo pa Kukula kwa Vuto la Kusoŵa Woceza Naye

Onani mmene anthu amene ali na vuto la kusungulumwa angapezele cimwemwe pali pano.

KHALANI MASO!

Kumene Mungapeze Ciyembekezo mu 2024—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Ciyembekezo cimene Baibo imapeleka cingakuthandizeni kukhala na umoyo wabwino pali pano komanso kuyembekezela tsogolo labwino.

KHALANI MASO!

Caka ca 2023 Cacititsa Anthu Ambili Kukhala na Nkhawa—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Baibo imafotokoza tanthauzo lenileni la zocitika za mu 2023.

Kodi Mungacite Ciyani Ngati Mumasoŵa Woceza Naye?

Onani mfundo ziŵili za m’Baibo zimene zingakuthandizeni ngati mumasoŵa woceza naye.

KHALANI MASO!

N’cifukwa Ciyani Cidani Caculuka?—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Onani cifukwa cake cidani cimene timaona masiku ano cili na tanthauzo lofunika, komanso zimene Mulungu adzacitapo.

Kodi Baibo Imatipo Ciyani pa Vuto la Madzi Padziko Lonse?

Ufumu wa Mulungu udzacita zimene maboma a anthu alephela kucita, udzacotsapo zonse zimene zimayambitsa mavuto a madzi amene tili nawo.

KHALANI MASO!

N’cifukwa Ciyani Anthu Akulephela Kukhazikitsa Mtendele?—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Onani zifukwa zitatu zimene zalepheletsa anthu kuthetsa nkhondo.

KHALANI MASO!

Kodi Ndani Adzapulumutsa Anthu?—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Baibo imakamba kuti Mulungu adzathetsa “nkhondo padziko lonse lapansi.” Motani?

KHALANI MASO!

Kodi Aramagedo Idzayambila ku Israel?—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Yankho lipezeka m’zimene Baibo imakamba pa nkhani ya Aramagedo.

Mavuto a Zacuma—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzacitapo Ciyani?

Kodi mudziŵa kuti Baibo imakamba za boma limene lidzathetsa mavuto onse a zacuma, kuphatikizapo kusiyana pakati pa anthu olemela na osauka?

Kodi Coonadi Cikali Cofunika Masiku Ano?

Baibo ingakuthandizeni kudziŵa coonadi m’dzikoli lodzala na nkhani zabodza.

Andale a Katangale—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzacitapo Ciyani?

Dziŵani mmene Mtsogoleli wa Ufumu wa Mulungu adzaonetsela kuti ni wodalilika komanso woona mtima, ndipo sacita zakatangale ngakhale pang’ono.

Zacilengedwe Zikuwonongeka—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzacitapo Ciyani?

Dziŵani mmene Ufumu wa Mulungu udzathetsela mavuto onse a zacilengedwe pa dziko lapansi.

Mavuto a Zaumoyo—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzacitapo Ciyani?

Dziŵani mmene Ufumu wa Mulungu udzabweletsela umoyo wabwino umene tifuna

KAMPENI YAPADELA

Nkhondo—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzacitapo Ciyani?

Dziŵani mmene Ufumu wa Mulungu udzabweletsela mtendele weniweni komanso citetezo.

Kodi Baibo Imatipo Ciyani pa Kusoŵa kwa Cakudya?

Mulungu sindiye amacititsa njala, koma anakambilatu za zimenezi.

KHALANI MASO!

Kusefukila kwa Madzi Kowononga—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Onani zimene tikuphunzilapo zokhudza masiku athu ano pa kusefukila kwa madzi kumene kukucitika pa dziko lonse.

KHALANI MASO!

Njala Padziko Lonse Yawonjezeka Cifukwa ca Nkhondo Komanso Kusintha kwa Nyengo—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Baibo imatipatsa malangizo othandiza, imatipatsanso ciyembekezo cakuti zinthu zidzakhala bwino.

KHALANI MASO!

Kutentha Koopsa pa Dziko Lonse mu 2023—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Baibo imakamba kuti Mulungu sadzalola kuti dziko lapansi liwonongeke kothelatu.

Kodi Baibo Imathandiza Bwanji Anthu Kukhala Ololela?

Malembawa aonetsa mmene Baibo imalimbikitsila mtendele na ulemu kwa anthu onse.

KHALANI MASO!

Mkulu Wina wa za Umoyo Wacenjeza za Mavuto Amene Acinyamata Amakumana Nawo pa Soshomidiya—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Onani mfundo zitatu za m’Baibo zimene zingathandize makolo kuteteza ana awo.

KHALANI MASO!

Ndalama Zopitilila $2 Tililiyoni Zawonongedwa pa Zida Zankhondo—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Baibo inakambilatu kuti maulamulilo amphamvu padziko lonse adzayamba kulimbilana ulamulilo, zimene zimapangitsa kuti awononge ndalama zambili.

Mmene Mulungu Amasamalila Anthu Amene Ali na Vuto Losamva

Padziko lonse anthu amene ali na vuto losamva akupindula na maphunzilo amene Mulungu akupeleka. Onani mmene zimenezi zikucitikila.

KHALANI MASO!

Makina Osewenza Ngati Munthu—Dalitso kapena Tsoka? Nanga Baibo Inenapo ciyani?

Baibo imaonetsa cifukwa cake anthu sangakhale otsimikiza kuti zopangapanga za makono zingagwilitsidwe nchito pa zinthu zothandiza zokha

Pindulani na Nsembe ya Yesu

Kodi ni zinthu ziŵili ziti zofunika zimene Yesu anatiphunzitsa kucita kuti tipindule na imfa yake?

KHALANI MASO!

Nkhondo ya ku Ukraine IIoŵa Caka Caciŵili—Kodi Baibo Ipeleka Ciyembekezo Cotani?

Dziŵani zimene Baibo inalonjeza kuti nkhondo zonse zidzatha.

KHALANI MASO!

Zivomezi Zamphamvu Zisakaza ku Turkey na ku Syria —Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Baibo imapatsa ciyembekezo na citonthozo kwa anthu amene akhudzidwa na zivomezi zosakaza zimene zacitika ku dziko la Turkey na Syria.

KHALANI MASO!

Asayansi Anafendezela Patsogolo Koloko ya Tsiku la Ciwonongeko—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Ngakhale kuti Baibo imakamba za mapeto, imatipatsanso ciyembekezo.

KHALANI MASO!

Zimene Zinacitikila Mboni za Yehova pa Cipululutso ca Nazi—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Anthu ambili amada nkhawa kuti mwina Cipululutso monga ca ulamulilo wa Nazi cingadzacitikenso.

KHALANI MASO!

Kodi Tsankho Pakati pa Mitundu Lingathe?—Nanga Baibo Imati Ciyani?

Masiku ano, anthu mamiliyoni akuphunzila kucokela m’Baibo mmene angamacitile mwaulemu na anthu anzawo.

KHALANI MASO!

N’cifukwa Ninji Zandale Zikugaŵanitsa Anthu Conco?— Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Kusagwilizana kwa anthu pa zandale kukuwonjezeka padziko lonse. Baibo imaonetsa yankho pa vutoli—mtsogoleli amene angagwilizanitse anthu onse.

KHALANI MASO!

Zifukwa Zokhalila na Ciyembekezo mu 2023—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Anthu ambili amayembekezela zinthu zabwino m’caka catsopano. Uthenga wabwino wa m’Baibo umatipatsa ciyembekezo codalilika.

KHALANI MASO!

2022: Caka ca Matsoka—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Baibo yokha ndiyo imafotokoza tanthuzo lenileni la zocitika zimenezi.

KHALANI MASO!

Kodi Mpikisano wa Cikho ca Padziko Lonse Ungagwilizanitsedi Anthu?—Baibo Ikutipo Ciyani?

Maseŵela olimbilana Cikho ca Padziko Lonse aloŵetsamo zambili osati cabe maseŵela.

KHALANI MASO!

Mudzasankha Ndani Kukhala Mtsogoleli Wanu?—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Mtsogoleli waumuntu ngakhale atakhala wocita bwino kwambili, amalephelabe mbali zina. Koma pali mtsogoleli mmodzi amene salephela mbali iliyonse.

KHALANI MASO!

Andale Akucenjeza za Aramagedo—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Kodi zida zanyukiliya n’zimene zidzayambitsa Aramagedo?

KHALANI MASO!

Kodi Akhristu Ayenela Kumenya Nkhondo—Nanga Baibo Ikambapo Ciyani?

Kodi Akhristu amene amamenyako nkhondo amatsatiladi malangizo a Yesu?

KHALANI MASO!

Kutentha Kodetsa Nkhawa Padziko Lonse—Kodi Baibo Ikambapo Ciyani

Kodi dziko lapansi lidzafika poti anthu sangakhaleponso?

KHALANI MASO!

Kuombelana Mfuti Kocititsa Kakasi Padziko Lonse—Kodi Baibo Ikambapo Ciyani?

Kodi pali ciyembekezo ciliconse kuti zaciwawa za conco zidzatha?

KHALANI MASO!

Dziko Lapansi Likuwonongedwa—Kodi Baibo Ikambapo Ciyani?

Vesi imodzi ya m’Baibo imavumbula zinthu zitatu zokhudza kuwonongedwa kwa dziko lapansi.

KHALANI MASO!

Kukwela Mitengo Kwa Zinthu Padziko Lonse-Kodi Baibo Imakambapo Ciyani?

N’cifukwa ciyani tikukumana na mavuto ambili a zacuma? Kodi Baibo ingatithandidze bwanji?

KHALANI MASO!

Kuwombela Anthu Mfuti M’masukulu—Kodi Baibo Ikambapo Ciyani?

Kodi n’cifukwa ciyani zocitika zankhanza zotelezi zimacitika? Kodi tingakhale na ciyembekezo cakuti zaciwawa zimenezi zidzatha?

KHALANI MASO!

Nkhondo ya ku Ukraine Iwonjezela Njala Padziko Lonse

Baibo inakambilatu kuti kudzakhala njala padziko lonse lapansi. Koma imapelekanso ulangizi wotithandiza mmene tiyenela kucitila nalo vutoli pali pano.

KHALANIBE MASO!

Anthu 6 Miliyoni Amwalila na COVID—Kodi Baibo Ikambapo Ciyani?

Baibo inanenelatu kuti kudzakhala milili yoopsa, komanso imatitonthoza pamene tikuvutika nayo, ndipo imatiunikila njila imene idzacotsapo milili yonse kothelatu.

KHALANIBE MASO!

Zimene Zipembedzo Zikucita pa Nkhondo ya ku Ukraine—Kodi Baibo Imati Ciyani?

Atsogoleli a machalichi kumbali zonse ziŵili za nkhondoyi akugwilitsa nchito mphamvu zawo mosemphana kwambili na zimene Yesu anaphunzitsa otsatila ake.

KHALANIBE MASO!

Vuto la Othaŵa Kwawo—Mamiliyoni Akuthaŵa m’Dziko la Ukraine

Baibo imafotokoza zoputila vutolo, komanso yankho lake lokhalitsa.

Russia Athila Nkhondo Ukraine

Dziŵani tanthauzo la cocitika cimeneci.

TSAMBA LOYAMBA

KAMPENI YOITANILA ANTHU KU CIKUMBUTSO

Yesu Adzacotsapo Anthu Osamvela Malamulo

Kodi tingaonetse bwanji kuti timayamikila zimene Yesu anaticitila komanso zimene adzaticitila m’tsogolo?

KAMPENI YOITANILA ANTHU KU CIKUMBUTSO

Yesu Adzathetsa Umphawi

Kodi tingaonetse bwanji kuti timayamikila zimene Yesu anaticitila komanso zimene adzaticitila mtsogolo?

KAMPENI YOITANILA ANTHU KU CIKUMBUTSO

Yesu Adzathetsa Nkhondo

Kodi tingaonetse bwanji kuti timayamikila zimene Yesu anaticitila komanso zimene adzaticitila mtsogolo?

Mmene Mulungu Amasamalila Anthu Amene Ali na Vuto Losamva

Padziko lonse anthu amene ali na vuto losamva akupindula na maphunzilo amene Mulungu akupeleka. Onani mmene zimenezi zikucitikila.

Zimene Baibo Ikambapo pa Kukula kwa Vuto la Kusoŵa Woceza Naye

Onani mmene anthu amene ali na vuto la kusungulumwa angapezele cimwemwe pali pano.

Kodi Baibo Imatipo Ciyani pa Vuto la Madzi Padziko Lonse?

Ufumu wa Mulungu udzacita zimene maboma a anthu alephela kucita, udzacotsapo zonse zimene zimayambitsa mavuto a madzi amene tili nawo.

Kodi Coonadi Cikali Cofunika Masiku Ano?

Baibo ingakuthandizeni kudziŵa coonadi m’dzikoli lodzala na nkhani zabodza.

Mavuto a Zacuma—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzacitapo Ciyani?

Kodi mudziŵa kuti Baibo imakamba za boma limene lidzathetsa mavuto onse a zacuma, kuphatikizapo kusiyana pakati pa anthu olemela na osauka?

Andale a Katangale—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzacitapo Ciyani?

Dziŵani mmene Mtsogoleli wa Ufumu wa Mulungu adzaonetsela kuti ni wodalilika komanso woona mtima, ndipo sacita zakatangale ngakhale pang’ono.

Zacilengedwe Zikuwonongeka—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzacitapo Ciyani?

Dziŵani mmene Ufumu wa Mulungu udzathetsela mavuto onse a zacilengedwe pa dziko lapansi.

Mavuto a Zaumoyo—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzacitapo Ciyani?

Dziŵani mmene Ufumu wa Mulungu udzabweletsela umoyo wabwino umene tifuna

KAMPENI YAPADELA

Nkhondo—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzacitapo Ciyani?

Dziŵani mmene Ufumu wa Mulungu udzabweletsela mtendele weniweni komanso citetezo.

Kodi Baibo Imatipo Ciyani pa Kusoŵa kwa Cakudya?

Mulungu sindiye amacititsa njala, koma anakambilatu za zimenezi.

Kusala Nyama olo Ciliconse Cocokela ku Zamoyo—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Onani ngati kusala nyama ni njila yothetsela mavuto pa dziko.

Kodi Baibo Imathandiza Bwanji Anthu Kukhala Ololela?

Malembawa aonetsa mmene Baibo imalimbikitsila mtendele na ulemu kwa anthu onse.

Pepani, palibe mawu olingana amene mwasankha.