Onani zimene zilipo

Cikumbutso ca Imfa ya Yesu

Kamodzi pa caka, m’madela ambili padziko lonse, timakumbukila imfa ya Yesu. Timacita zimenezi cifukwa iye analamula otsatila ake kuti: “Muzicita zimenezi pondikumbukila.”—Luka 22:19, 20.