Pitani ku nkhani yake

Nkhani Zomwe Zangoikidwa Kumene Patsamba Loyamba la Webusaiti Yathu

 

Kodi Mudzasankha Ndani Kukhala Mtsogoleri Wanu?​—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Ngakhale olamulira ena amakhala abwino, koma ali ndi malire. Pali Mtsogoleri mmodzi yekha yemwe tingamudalire.

Samalani Kuti Musamapusitsike Ndi Nkhani Zabodza

Musamangokhulupirira zilizonse zimene mwamva kapena kuwerenga. Dziwani zimene mungachite kuti musamapusitsidwe ndi nkhani zabodza.

Kodi ndi Zotheka Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu?

Kodi munaganizapo zomufunsa Mulungu kuti: “Kodi ndinu ndani? Mumakhala kuti? Kodi mumasamala zokhudza ine?”

 

Kodi Dzikoli Lidzakhalanso Bwino?​—⁠Nyanja Zikuluzikulu

Kodi nyanja zimene zawonongedwazi zingakonzedwenso?

Mungatani Kuti Muchepetse Nkhawa?

Onani njira zomwe mungatsatire kuti musamakhale ndi nkhawa kapena kuti mukwanitse kuzichepetsa.

Anthu Sakumvera Malamulo Padziko Lonse

Kodi Baibulo Limanena Zotani?

 

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani Yogonana Amuna Kapena Akazi Okhaokha?

Kodi Mulungu amaona bwanji anthu ogonana amuna kapena akazi okhaokha? Kodi zingatheke kuti munthu amene ali ndi mtima wofuna kugonana ndi amuna kapena akazi anzake ayambe kuchita zinthu zosangalatsa Mulungu?

Kodi Mulungu ndi Amene Amachititsa Kuti Tizivutika?

Anthu ambiri amasokonezedwa ndi ziphunzitso zabodza zokhudza Mulungu. Kodi zoona zake ndi ziti?

Kodi Mungadziwe Bwanji Choyenera ndi Chosayenera?

Kodi mungasankhe bwanji? Nanga malangizo odalirika okuthandizani kusankha moyenera mungawapeze kuti?

 

Kodi Mulungu Amaganizira Akazi?

Yankho la funso limeneli lingakuthandizeni kupeza mtendere pamene mukuchitiridwa nkhanza kapena zinthu zina zopanda chilungamo chifukwa choti ndi mkazi.

 

Kodi Anthu Adzasiya Liti Kumenya Nkhondo?​—Zimene Baibulo Limanena

Posachedwapa nkhondo zonse zidzathetsedwa. Baibulo limafotokoza mmene zimenezi zidzachitikire.

Kodi Aramagedo Idzayambira ku Isiraeli?

Kodi Baibulo limanena zotani?

 

Muzithandiza Ena Polimbana Ndi Maganizo Odziona Kuti Muli Nokhanokha

Malangizo ochokera m’Baibulo angakuthandizeni.

 

Samalani Kuti Musamapusitsike Ndi Nkhani Zabodza

Nkhani zosocheretsa, malipoti abodza ndi mphekesera zafala kwambiri ndipo zingakubweretsereni mavuto.

Mungakhale ndi Moyo Wosangalala

Magaziniyi ya Galamukani! Ikufotokoza mmene malangizo anzeru a m’Baibulo angakuthandizireni.

 

Kodi Sayansi Imagwirizana ndi Baibulo?

Kodi m’Baibulo muli mfundo zolakwika zokhudza sayansi?

Mulungu Wachikondi Adzatipatsa Madalitso Osatha

Werengani kuti mudziwe madalitsowa, chifukwa chake mungawakhulupirire komanso mmene mungawapezere.