Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kodi N’zotheka Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu?

Kodi N’zotheka Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu?

Atate wathu wachikondi akuitana onse omwe amamufunafuna kuti akhale nawo pa ubwenzi. Kodi inunso mukufuna kukhala naye pa ubwenzi?