Onani zimene zilipo

Mulungu

Kodi Mulungu Ndani?

Kodi Mulungu Alikodi?

Baibo imayankha mwa kupeleka maumboni asanu okhutilitsa.

Kodi Mulungu Amapezeka Pena Paliponse?

Kodi Baibo imaphunzitsa kuti Mulungu amapezeka pena paliponse? Mungakhale wotsimikiza bwanji kuti Mulungu ali na malo ake-ake amene amakhala, ndipo amakudziŵani bwino inuyo panokha?

Kodi Mulungu Amasintha Maganizo Ake?

Kodi Baibo imadzitsutsa ikamanena kuti Mulungu anati, ‘Ine sindisintha’ komanso kuti, “Ndidzasintha maganizo anga”?

Kodi Mzimu Woyela N’ciani?

Pa cifukwa comveka, Baibo imachula mzimu woyela kuti “manja” a Mulungu.

Dzina la Mulungu

Kodi Yehova N’ndani?

Kodi iye ni Mulungu wa mtundu umodzi wa anthu, monga Aisiraeli?

Kodi Mulungu Ali na Maina Angati?

Anthu ena angaganize kuti maina a Mulungu ni ‘Allah’ kapena ‘El Shaddai,’ komanso ‘Yehova-Yire’ kapena ‘Alefa ndi Omega.’ N’cifukwa n’ciani n’kofunika kudziŵa maina amene timaseŵenzetsa pochula Mulungu?