Pitani ku nkhani yake

Pemphero

Why Pray?

Kodi Kupemphera N’kothandizadi?

Mulungu angayankhe pemphero la munthu popanda kuchita zozizwitsa.

Kodi Mulungu Amamva Mapemphero Athu?

Baibulo limatitsimikizira kuti Mulungu amamvetsera mapemphero athu tikamapemphera m’njira yovomerezeka.

Kodi Mulungu Angayankhe Mapemphero Anga?

Kuti Mulungu ayankhe mapemphero anu zimadalira kwambiri pa zimene inuyo mumachita.

Mmene Ndingapempherere

Kodi Mungatani Kuti Mulungu Azimvetsera Mapemphero Anu?

Tikhoza kulankhula ndi Mulungu kulikonse, nthawi iliyonse, mokweza kapenanso chamumtima. Ndipotu Yesu anatithandiza kudziwa zomwe tinganene popemphera.

Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani ya Pemphero

Kodi tiyenera kumapemphera kwa angelo komanso kwa oyera mtima?

Kodi Ndingatchule Zinthu Ziti Popemphera?

M’nkhaniyi muona kuti Mulungu saona kuti nkhani ngati zimenezi ndi zazing’ono.

Muzipemphera Kuti Mulungu Akudalitseni

Kodi tingapemphere bwanji kuti Mulungu azimva mapemphero athu komanso kutidalitsa?

N’chifukwa Chiyani Mulungu Samvetsera Mapemphero Ena?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mapemphero amene Mulungu sayankha komanso anthu. Mudziwanso anthu amene Mulungu sawamvetsera akamapemphera.

Kodi Tizipemphera kwa Yesu?

Yesu anatiuza yankho la funso limeneli

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupemphera M’dzina la Yesu?

M’nkhaniyi muona kuti kupemphera m’dzina la Yesu kumasonyeza kuti timalemekeza Mulungu komanso Yesu.

Kodi Ndizipemphera kwa Anthu Oyera Mtima?

Dziwani zimene Baibulo limanena pa nkhani yakuti tizipemphera kwa ndani.