ZOTI MUCHITE Mmene Kutumizirana Zithunzi Kungakhudzire Mbiri Yanu YAMBANI Zoti muchitezi zikuthandizani kuti muzikhala osamala musanatumizire ena zithunzi. Pangani Dawunilodi Nkhani Zina Zoti Achinyamata Achite Achinyamata Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani pa Nkhani Yotumizirana Zithunzi pa Intaneti? Kuika zinthu zimene zimakusangalatsani pa intaneti ndi njira yabwino yolumikizirana ndi anzanu komanso anthu a m’banja lanu, koma kukhoza kukhalanso koopsa. MAVIDIYO AMAKATUNI Muzichita Zinthu Mosamala Mukamacheza ndi Anzanu pa Intaneti Chitani zinthu mosamala mukamacheza ndi anzanu pa Intaneti. ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Kukhala Munthu Wotchuka pa Intaneti Kuli Ndi Phindu? Anthu ena amalolera kuika moyo wawo pangozi n’cholinga choti akhale ndi anthu ambiri owatsatira komanso okonda zimene aposita pa intaneti. Kodi kukhala wotchuka pa intaneti n’kothandizadi? ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Malo Ochezera a pa Intaneti Akusokoneza Moyo Wanga? Malo ochezera a pa intaneti amakomedwetsa. Mfundo zotsatirazi zikuthandizani kuti muzidziletsa. Patsani ena Patsani ena Mmene Kutumizirana Zithunzi Kungakhudzire Mbiri Yanu ZOTI ACHINYAMATA ACHITE Mmene Kutumizirana Zithunzi Kungakhudzire Mbiri Yanu Chichewa Mmene Kutumizirana Zithunzi Kungakhudzire Mbiri Yanu https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502017140/univ/art/502017140_univ_sqr_xl.jpg