Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Moyo Wanga Wachinyamata​—Ndingatani Kuti Ndikonze Zomwe Ndinalakwitsa M’mbuyo?

Moyo Wanga Wachinyamata​—Ndingatani Kuti Ndikonze Zomwe Ndinalakwitsa M’mbuyo?

Thalila ndi José anazindikira kuti munthu akachita cholakwika chimodzi sizivuta kuchitanso zolakwika zina. Kodi iwo anachita zotani kuti apewe kulakwitsanso zinthu zina?