Zatsopano pa JW.ORG

2024-06-03

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU

September–October 2024

2024-05-22

KHALANI MASO

N’chifukwa Chiyani Makhalidwe Abwino Alowa Pansi?—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Makhalidwe abwino alowa pansi kwambiri panopa. Baibulo limafotokoza chifukwa chake makhalidwe abwino alowa pansi komanso lili ndi malangizo omwe angathandize anthu kukhala ndi makhalidwe abwino.

2024-05-22

ANTHU OKWATIRANA KOMANSO MABANJA

Kodi Tiyambe Kukhala Limodzi Tisanakwatirane?

Anthu ena amaganiza kuti kuyamba kukhala limodzi kaye asanakwatirane kungawathandize kukonzekera banja. Kodi amenewa ndi maganizo abwino kapena pali njira ina yabwino?

2024-05-22

ANTHU OKWATIRANA KOMANSO MABANJA

Mungatani Kuti Mupewe Kuthetsa Banja Pambuyo Pokhala Limodzi kwa Zaka Zambiri?

N’chiyani chikuchititsa kuti anthu azithetsa banja pambuyo pokhala limodzi kwa zaka zambiri? Kodi mungatani kuti zimenezi zisakuchitikireni?

2024-05-20

NYIMBO ZA BROADCASTING

“M’dziko Labwino”

Kuganizira kwambiri za chiyembekezo chathu kumatithandiza kupirira ngakhale mavuto aakulu.