Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

“M’dziko Labwino”

“M’dziko Labwino”

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. Moyo wabwino, ngati kutulo, tili m’dziko labwino.

    Imfa yagonja nkhawa zonse zatha!

    Takhalanso angwiro.

    Zonse zomwe tikuona, n’zosangalatsa.

    Yehova watipatsadi, mphatso zabwino.

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Panopa tikudikirabe

    (KOLASI)

    Pomwe tidzatukula mitu yathu ndi kupulumuka.

    Yehova ’dzatipukuta m’sozi m’maso mwathumu.

    M’dziko labwino.

  2. 2. Mwayi wathu timangeko nyumba M’lungu watidalitsa.

    Njala yatha, chakudya paliponse ngakhaletu m’mapiri.

    Kulira titaiwala, zosangalatsa!

    Mavuto onse atatha, atatha, atha!

    (KOLASI)

    Pomwe tidzatukula mitu yathu ndi kupulumuka.

    Yehova ’dzatipukuta m’sozi m’maso mwathumu.

    M’dziko labwino.

    (VESI LOKOMETSERA)

    Panopa chiyembekezo chathuchi chikule.

    Pompano Tilowa m’dziko labwino Lokoma.

    (KOLASI)

    Pomwe tidzatukula mitu yathu ndi kupulumuka.

    Yehova ’dzatipukuta m’sozi m’maso mwathumu.

    (KOLASI)

    Tidzatukuladi mitu yathu ndi kupulumuka.

    Yehova ’dzatipukuta m’sozi m’maso mwathumu.

    M’dziko labwino.

    (MAWU OMALIZA)

    Pompano—pompano

    Zitheka.

    Pompano—pompano

    Tilowa.

    Pompano—pompano

    Zitheka.

    Pompano—pompano

    Tilowa.