NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA July 2024
Magazini ino ili na nkhani zophunzila mu mlungu wa September 9–October 6, 2024.
NKHANI YOPHUNZILA 27
Khalani Wolimba Mtima Monga Zadoki
Yophunzila mu mlungu wa September 9-15, 2024.
NKHANI YOPHUNZILA 29
Khalani Maso Kuti Musagonje pa Mayeselo
Yophunzila mu mlungu wa September 23-29, 2024.
NKHANI YOPHUNZILA 30
Maphunzilo Ofunika Amene Titengapo Kwa Mafumu Aciisiraeli
Yophunzila mu mlungu wa September 30–October 6, 2024.
Zimene Zingakuthandizeni Mukasamukila mu Mpingo Watsopano
Akhristu ambili akwanitsa kuzoloŵela mpingo watsopano. N’ciyani cimathandiza munthu kuzoloŵela mpingo watsopano? Onani mfundo zinayi zimene zingakuthandizeni.
Mafunso Ocokela kwa Oŵelenga
Kodi “mkazi” wochulidwa pa Yesaya 60:1 ndani, nanga ‘adzaimilila’ motani, ndipo ‘adzaonetsa kuwala kwake’ motani?