Onani zimene zilipo

JULY 15, 2022
NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Ciunikilo Na. 5 ca Bungwe Lolamulila mu 2022

Ciunikilo Na. 5 ca Bungwe Lolamulila mu 2022

Wa m’Bungwe Lolamulila akupeleka lipoti la zocitika zosangalatsa zaposacedwa zokhudza nchito yomasulila na zipambano za kukhoti. M’ciunikiloci mulinso mbali yolimbikitsa, yoonetsa abale na alongo akufotokoza zimene zinawathandiza kupilila cizunzo mu ulamulilo wakale wa Soviet Union.